@user8138712982736: 🔐 YATSANI REQUIRE PASSWORD TO POWER OFF! PA PHONE YANU ISANABEDWE “Kodi mukudziwa kuti munthu akhoza kuizimitsa phone yanu ikabedwa? 😳 Yatsani setting iyi kuti password ifunike musanayimitse phone!” Phone ikabedwa kapena kutayika, wakuba angayesetse kuizimitsa kuti zikhale zovuta kuipeza. 📱🚨 Mu phunziro ili ndikukuwonetsani mmene mungayatsire Require Password to Power Off kuti phone yanu ifunike PIN kapena Password munthu akafuna kuiyimitsa pamene ili locked. 🔐 ⚠️ Kumbukirani: Setting imeneyi sipezeka mofanana pa ma phone onse, ndipo ma steps amasiyana malinga ndi mtundu wa phone komanso software version. 👇 Onani Comment Section kuti muone ma steps a mitundu yosiyanasiyana ya ma phone! #PhoneSecurity #TheftProtection #AndroidTips #PhoneTips #youngmalawiancoach

Hendrison Kathumba
Hendrison Kathumba
Open In TikTok:
Region: ZA
Wednesday 02 September 2026 14:53:40 GMT
3667
48
5
2

Music

Download

Comments

user571552262769
ishamu kendo :
Hawai
2026-09-02 20:10:07
0
user12983711613723
secret :
ma text a fon ina azifikaso mu fon ina km Yama Keypad
2026-09-02 15:09:09
0
user1435660126761
إبراهيم بن ووش :
pangani ya oppo
2026-09-02 16:17:47
0
user8138712982736
Hendrison Kathumba :
📌 MA PHONE NDI MA STEPS A REQUIRE PASSWORD TO POWER OFF 🔐📱 ⚠️Dziwani: Ma settings amasiyana malinga ndi model ya phone komanso software version. Ngati simukupeza njira yomwe yalembedwa pansipa, gwiritsani ntchito Search mu Settings ndikulemba Power off password, Turn off verification kapena Power off. ━━━━━━━━━━━━━━━━━━ 📱 OPPO Settings → Security & privacy → More security & privacy → Require password to power off → ON ━━━━━━━━━━━━━━━━━━ 📱 OnePlus Settings → Security & privacy → More security & privacy → Require password to power off → ON ━━━━━━━━━━━━━━━━━━ 📱 HONOR Pa ma HONOR ena: Settings → HONOR ID / Account Center → Find Device → Turn-off verification password → ON ━━━━━━━━━━━━━━━━━━ 📱 SAMSUNG Pa Samsung ambiri, option ya Require password to power off ikhoza kusapezeka monga momwe ilili pa OPPO kapena OnePlus. Koma yatsani: Settings → Lock screen and AOD → Secure lock settings → Lock network and security → ON Izi zimathandiza kuletsa kusintha make network ndi ma security settings ena pamene phone ili locked. ━━━━━━━━━━━━━━━━━━ 📱 XIAOMI / REDMI / POCO Ma Xiaomi/Redmi/POCO ambiri alibe option yeniyeni ya: Require password to power off Choncho yang'anani njira zina monga: Settings → Google → All services → Find Hub Kapena: Settings → Google → Theft Protection ━━━━━━━━━━━━━━━━━━ 📌 Ngati mtundu wa phone yanu sunatchulidwe apa, comment mtundu wa phone yanu ndi Android/software version yake. Ma steps amasiyana pa ma phone ndi ma software version osiyanasiyana. 🔐📱
2026-09-02 14:54:31
0
To see more videos from user @user8138712982736, please go to the Tikwm homepage.

Other Videos


About