achotseni onsee ophunzila ndi ambiri ngakhale ine ndikadali kutari komaso ndineso wophunzira chotsani anthuwo
2026-09-03 06:55:03
0
Maria Phiri :
700 mzuzu
2026-09-03 07:35:14
0
T. liweta :
Izizi musamachite kupanaga announcement muziwazizimusa mu ma offices ngati momwe ankachitira former VP manganya 😂
2026-09-03 07:24:04
0
kelz mose :
ndipo ku Malawi anthu tikulangana ☺️☺️☺️
2026-09-03 07:37:15
0
dmtambalaikaM@ :
Anthu mu government ambiri apanga overdue. Anthu ambiri akayenera kuchotsedwa ntchito. Anthu sakupanga deliver there no need to keep them. Munthu azisungidwa ndi performance yake.