@anthu.aku.lilongwe: Zili ku Lilongwe Area 49 Dubai anthu apwetekedwa ndi mkulu wina yemwe pakadali pano sakudziwika Akafika mbari yakwanuko chonde tidziwitseni Follow Anthu aku Lilongwe

Anthu aku Lilongwe
Anthu aku Lilongwe
Open In TikTok:
Region: MW
Thursday 03 September 2026 09:35:17 GMT
131817
4430
595
750

Music

Download

Comments

user1915196974374
Beatrice :
ndipo ine ndili Khan yanga 🤣 yangat yomwey mhuuuuu
2026-09-07 11:01:08
0
user33707911355660
Ceĺine 💚❤️💛🩷💞 :
Next time speak fast fast .zochita zimachuluka pa fon pa😂
2026-09-06 15:21:41
14
user514097227761
cynthia daniel :
🤣🤣🤣🤣🤣 km anthu
2026-09-07 12:23:12
0
memoh416
Memoh :
😂😂😂😂 Ndpo live
2026-09-07 20:24:50
0
carolinelombola53
carolinelombola53 :
zikomo mwa chenjeza asanafike kudela lakwanthu kuno mmmmmm
2026-09-07 09:00:29
1
user9504110350758
yahaya Lamecki :
Mmm Amalawi kutengeka esh 😭😭🇿🇦
2026-09-06 15:29:44
1
user21006205996808
Ticia💕 :
ndudandaula mamuna wanga ndotengeka 😄
2026-09-04 05:39:17
31
shamima.isa
Shamima Isa :
ali ndi makhwala achipha ntima ameneyo
2026-09-04 10:10:34
10
user3815010622035
memory chopi :
koma makani Ali ndine sure bwezi ndatembenuka aaah
2026-09-03 18:06:43
22
ellenchimtengo737
Ellen Chimtengo :
good explanation
2026-09-03 20:17:23
20
user1547817524777
loveness 04 :
🤣🤣🤣🤣🤣 Ine zandipaniphonya Pati komwe kuno ku Dubai
2026-09-04 05:00:14
10
emmanueljames9695
Emmanuel James :
Dubai Malawi emwey?
2026-09-03 20:09:16
13
dtee2026
DTEE RENT A CAR :
koma athu a ntown mwenimweni mpaka kupangidwa zimenezo??😂😂😂 eish ndalama ili pamingadi eti
2026-09-03 20:58:22
6
mariam.isaac527
Emily Issac :
Malawi 🇲🇼 Malawi 🇲🇼 Malawi 🇲🇼 ndaitana kangati ine omhoo muzasukusula liti kutengeka ndizina zilizonse umphawi utipwetekesa😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂 why My country 😂😂😁
2026-09-03 17:03:16
8
ishmaelpaladwe
Ishmael Paladwe :
osamalemba zochedwetsa anthu zochita
2026-09-03 10:44:17
5
user9923186240515
user9923186240515 :
ndifunse anzanga a shop ku msika ndimvetse
2026-09-03 19:51:24
5
innocencia198
user7540159329238 :
kudubai kwake kwathu komkuno 🥹😆😆😆 zandisempatu ine
2026-09-03 21:00:22
6
sapesah4
SAM PATIENCE MAJAMANDAH :
nyimb ikuveka pasi pasi yo anayimb NdAn
2026-09-04 03:47:31
6
user8883873723217
happie :
zimezo sizinga chitike ku Blantyre
2026-09-04 07:23:54
5
eva.k55
Eva K :
umphawii sizithu inu
2026-09-03 18:19:50
5
haroonharold
Haroon Harold :
manda aku mvama pali police why sanapite
2026-09-03 18:50:45
5
fernandeznehemiah
Fernandez808 :
Fact bro and one of them is my customer
2026-09-04 21:09:54
1
user3404317858111
Clara💞 :
😂😂😂😂😂koma ndaseka eee kumanda amvama mpakana kuonetsana malibwada😂😂🙆
2026-09-04 14:44:48
2
jimmy.nkhoma4
jimmy nkhoma :
ine ndili kuno ku Dubai bwanji sindinamve kumangonena zabbodza
2026-09-04 07:33:31
1
To see more videos from user @anthu.aku.lilongwe, please go to the Tikwm homepage.

Other Videos


About