@manda00072: #malawiantiktok🇲🇼 #chilimainquiry #goviral #fyppppppppppppppppppppppp #malawi

User MANDA🇬🇧🇲🇼🇿🇲
User MANDA🇬🇧🇲🇼🇿🇲
Open In TikTok:
Region: MW
Thursday 03 September 2026 15:40:29 GMT
185782
6742
170
235

Music

Download

Comments

lisabelliora
Liora🇲🇼 :
ine ndimaganiz kuti mu ndege alipo anthu ena ake amadziwa ma plan ndipo anthu amenewo sanafe mawo
2026-09-16 23:06:28
57
lindajereharmony
Linda Jere harmony :
zomvetsa chisoni kuti anthu ambiri ankaziwa kuti anthuwa sakabwera😳
2026-09-16 18:00:43
35
djemba491
Jacked Djemba :
Why are we wasting time kodi…mesa we have prophets kodi?Abwele atiwuze what really happened
2026-09-30 10:58:14
4
lusychell3
Lusychell 03 :
Moti apopo amkapit kokufa 😭😭😭😭😭😭
2026-09-03 18:23:17
52
dumisani.aron.geb
Dumisani Aron Gebashe :
CCTV siwonetsa mkati mwa ndege unless mndegemo munali camera
2026-09-03 20:44:27
11
ccovh8
SHAIBU CHAKWAMBA :
Let by goes be by goes nothing can change the situation...let HIM above to be him
2026-09-03 18:52:32
17
user8138712982736
Hendrison Kathumba :
Akuonesa malo amodzi bwanji ngat CCTV Inaliko ndi imodzi yokha
2026-09-03 17:33:39
7
elickjackson543
elickjackson543 :
akudziwa umboni ose olanga ndi mulungu
2026-09-03 21:06:22
9
bofyo1
chi Bofyo.. :
kulowa osaziwa.. ndimathero.. 😭😭
2026-09-18 20:47:03
0
shadricktukuragmail.com
promise :
koma nchifukwa chani ku malawi kuno zonse ndizokanika bwanji atsogoleri athu tazikhalani ndi manyadzi dzikoli simumalikonda ayi mpaka pa airport 🛫 kumalephera chitetezo chokwanira mmmmmmm
2026-09-19 06:56:07
1
qassimtwalibu
786 TK M'DELEMAN GROUP :
ngakhale CCTV inajwmbula kose koma musaiwale kuti unali ulamulilo wa mcp ndi athu oke anapanga chipongwe chakupha athuwo zachiziwikileni kuti anapanga delete zose
2026-09-13 08:59:00
8
cosmasmagwazeni
cosmasmagwazeni🇲🇼 :
I don't know kuti ma guy awawa ati afufuza zichani, my point is ma guy awawa afuna apezebe wina wake kuti ndiolakwa basi, nanga CCtv ndikuchikangawa zugwilizana bwanji
2026-09-10 09:59:55
3
user28034992790307
user28034992790307 :
mcp inapha athu 9 mosakayikisa
2026-09-17 04:34:10
6
mr.cool83190
MR COOL :
at adalibe chiyembekezo kuti pakhala loopholes so what is the meaning of security 🤷 anytime anything can happen pake Pali chitetezo palibe kupuma that why kuli 24/ 7 shifts guard
2026-09-23 14:47:40
1
nellie2761
Nellie@@ :
plot ya asilikali iyi
2026-09-16 07:13:06
5
user2492814138427
user2492814138427 :
kod inu a mcp mumaganiza kuti anthu munawapha aja mungapeze mtendele?Pali mwazi wamunthu chilungamo chimabwela
2026-09-17 08:21:32
5
patience.mmadi
Patience Mmadi :
Ulendo osakabweleraso Ooh God😭😭😭😭😭😭😭😭😭
2026-09-23 00:14:47
1
wil4rd3
Wil4rd :
CCTV ngati inajambula zolakwika zimene anthu oyipawo sankafuna kuti paoneke ndekuti apanga delete .. inu ndianthu oyipa osewo .
2026-09-04 16:34:01
9
user5150591611520
bella isabella85 :
chotseniko umbuli ndine wakwamsakambewa kudowa ma parachute aja amagwilitsidwa ntchito nthawi itiyo?
2026-09-18 07:43:24
4
giftmagwira20
Gift Magwira :
apa tidabwepo
2026-09-18 20:06:26
2
247bull
NG'OMBEZ Meyerdy :
Inu nkhn iy mpk 2090
2026-09-10 20:06:15
3
mr.chidetsa
Memory chidetsa :
Cctv ngati ili mitambo
2026-09-16 21:31:23
2
dollahvdbanda
Dollah Vd Banda :
ma umboni akuoneseratu kuti their is something need to be fished out
2026-09-16 09:38:38
3
thomas.masebwe
Thomas Masebwe :
follow
2026-09-15 19:04:45
2
owenpotani596
Owen Potani :
ationetseso mene ndege lnafikila mpakana apa anafika avp
2026-09-04 05:53:14
3
To see more videos from user @manda00072, please go to the Tikwm homepage.

Other Videos


About