@prophetpaulangel: #onthisday #tanzania🇹🇿 #malawitiktok🇲🇼 #zimabwetiktok🇿🇼🇿🇼🇿🇼🇿🇼 #southafricatiktok🇿🇦

Prophet paul angel 🇲🇼
Prophet paul angel 🇲🇼
Open In TikTok:
Region: MW
Sunday 06 September 2026 17:53:16 GMT
32234
1806
283
142

Music

Download

Comments

chikumbutso30
Grace phiri🇲🇼🇲🇼🇲🇼 :
ndipo zoona
2026-09-15 07:38:07
0
essieh75
Esme :
nde Pali amuna ena kukhumudwisa mkaz saonapo Vuto olo azilila amaona ngat opepela akut nde Amati ngat mulungu anandidalisa sangandilande fukwa cha misozi yakoyo ambuye achite nawo anthu amenewa ndinthu
2026-09-07 05:00:49
11
user4798258031956
faith c miliano :
ndipo zoona ine ndadutsa naye mu nyengo zowawa pano mulungu anawadalitsa pano akut ndine osafunikira, mulungu achite nawo amuna oterewa
2026-09-14 06:41:45
1
macksonsaiden
macksonsaiden :
ndipo ine ndinalila kutopa
2026-09-08 10:12:53
3
fatimamatemba588
Fatima Matemba :
amen amen ine narandidwa chirichonse koma ndadusa naye munyengo zowawa koma misozi yanga singathere mwaurere kumwamba Mulungu aripo😭😭😭😭
2026-09-07 03:06:54
3
joymadakaa
user2399151039499 :
ma coment ali apa zikuonetsa zinthu sizili bwino shaaaa
2026-09-08 11:57:13
1
eliza.mwanga3
Eliza mwanga :
Amen ineyo nditasiyana ndi chibwez changa ndinali la kwambili sipanathe miyez itatu akuzuzika kwambili
2026-09-06 19:24:08
2
anne.msasa
Faith 998 :
Amen,koma zimenezi samadziwa
2026-09-06 18:56:36
4
tionge2709
Tionge :
amunaa eee amaminisatuu ukonde kwambili mmm walakwisa yimakhara heartbreak siyamasewera mtima kusiya kugunda eee
2026-09-08 18:58:08
1
alinafe639
Alinafe :
exactly prophet Paul 🔥🔥🔥🔥
2026-09-08 09:42:15
1
jenara.daud
Jenara Daud :
Nena iwe,,zirikuno ndipo ndimakhulupirira
2026-09-07 21:07:27
1
agnesluwis281
agnesluwis281 :
amen and amen and amen
2026-09-06 19:08:13
2
25tiyanjane
Tiyanjane :
Ine pano ndinalila
2026-09-07 18:22:09
1
user1222616198066
user1222616198066 :
mamuna wina zazizika moyo wake onse
2026-09-07 09:30:10
2
trizahlihaka1
trizah :
eeeeeeee amuna ine
2026-09-07 08:18:54
1
limbikanikastom
Limbikani Kastom :
Amen and amen
2026-09-08 04:09:13
1
charityzulu716
charity :
Yeah
2026-09-07 11:35:34
2
maggiephiri870
Maggie Phiri :
amen amen amen amen 🙏🙏🙏🙏
2026-09-06 20:14:02
2
lekisachayaka
Lekisa Chayaka🙏🙏🙏 :
amen ine ndalila kom ndatopa ndingoyang,ana kwayesu basi
2026-09-07 19:49:58
1
agiemakhaya
phioma :
9months kumangolila dzko lawen koma mulungu akuona😭😭😭
2026-09-06 18:43:17
2
faytcheso
Fay Tcheso :
Amuna ena ndi amfiti 💔
2026-09-14 11:16:14
0
mathapelo18chirwa
Nomthandazo :
Amen
2026-09-12 21:46:31
0
mathapelo18chirwa
Nomthandazo :
en
2026-09-12 21:46:21
0
fatimamw7
fatimamw7 :
amen
2026-09-12 18:58:15
0
tione.mayula
tione mayula :
Zoona pastor
2026-09-13 21:17:28
0
To see more videos from user @prophetpaulangel, please go to the Tikwm homepage.

Other Videos


About