@moseschikolosa: Kusangalala ndi chisankho! Nthawi zambiri timakhala moyo umene sitimaufuna chonsecho moyo wathu ndi chopembedzera cha ena: Enafe ndife ochepa thupi ndipo sitimafuna mkomwe tikuoneka m'mene tiriri chonsecho, ena amafuna atakhalanso ochepa thupi ngati ife! Ena timafunitsitsa titakhala moyo uwo kapena uwu kuti tidzakhale osangalala koma ayi ndithu! Kusangalala ndi chisankho- Sitimakhala osangalala chifukwa cha kupeza zimene timazifuna koma tikhoza kukhala osangalala pofuna zimene tinazipeza! 1. Alipo okwatira amene amkaona ngati adzasangalala akapeza banja koma lero ayi ndithu! 2. Alipo ena amkaona ngati adzakhala osangalala akadzapeza ana koma ayi ndithu mtendere alibe! 2. Alipo ena amkaona ngati adzasangalala akadzapeza ntchito kapena chuma, lero mtendere alibe...
Moses Chikolosa
Region: MW
Thursday 10 September 2026 07:28:31 GMT
Music
Download
Comments
Victoria Mwalilino :
zikomo abusa ndimau amphabvu amen
2026-09-25 04:55:45
1
GLADYS PHIRI :
ameeeeeen and ameeeeeen
2026-09-19 06:58:09
1
Nyasa Landmw :
that's true amen pastor
2026-09-17 02:48:31
0
Joe Zongocheza :
Amen and Amen
2026-09-15 15:34:31
0
Grace Jere :
ndipo ndizoonadi munthu wamulungu,, word of wisdom
2026-09-22 12:29:23
0
Coleta Raphael jumbo :
amen amen
2026-09-15 17:05:46
0
clementinamakawa1 :
wow amen this is 100Percent true in short tizikhutisidwa kumayamika pomwepo tili sizonse zomwe tingazipeze mmoyowu zonse tilinazo Mulungu anatiyeneleza nazo dnipo anaziwa kuti zitikwanila
2026-09-12 08:12:41
1
Dee~kay :
Ameeeen
2026-09-15 09:54:28
0
Evans Kajawo :
mbale talimbikitsika ndimauamenewa ambuye akalemekezeke
2026-09-19 04:42:48
0
natasha :
amen ndpo zofuna sizithai
2026-09-14 06:20:31
0
chinsisi padambo :
Amen
2026-09-15 10:36:59
0
nizia607 :
eeeh Amen
2026-09-19 12:03:44
0
wide sper mw :
amen
2026-09-17 15:17:39
0
OK :
amen 🙏 🙏
2026-09-15 20:35:27
0
Banda Lydia :
Amen🙏🙏
2026-09-10 08:14:42
0
me :
Amen
2026-09-19 03:59:28
0
Eusébio Felizardo Foliass :
amen
2026-09-15 15:10:14
0
elicychisale :
amen
2026-09-15 13:44:50
0
Yamikan :
Emen
2026-09-11 09:17:44
0
user4213365134736 :
Amen 🙏
2026-09-11 06:57:41
0
Luwiza Gunde :
emeniii 🙏🙏
2026-09-11 05:22:43
0
Elisy :
Amen
2026-09-11 04:50:07
0
ndy ifeyo 😎 :
Amen
2026-09-11 04:17:31
0
AGNESS SAIDI :
Amen 🙏
2026-09-10 19:10:28
0
Tiamike mbalati :
ndiponso Amen
2026-09-10 08:23:06
0
To see more videos from user @moseschikolosa, please go to the Tikwm
homepage.
© 2021-2026 TikWM. All rights reserved.