@alexsndergombar:

alexsndergombar
alexsndergombar
Open In TikTok:
Region: MW
Thursday 10 September 2026 09:41:06 GMT
5540
97
68
35

Music

Download

Comments

savelightnkhoma3
Savelight Nkhoma :
anthuwa ndi akuba ndi chifukwa chake sindipita Ku church because church it's a business what am I gaining to go the church. if I go to church I must invest so that when am down church must lift me up
2026-09-13 11:29:11
2
user3071144829462
Cool :
I have said this over and over. This is the fall of my Parent church.
2026-09-14 08:47:40
1
charleskamwendo34
gogo Biyeni :
You just missed a point elder Gombwa. Tithe is not for the purposes that you mentioned. Offerings are for such. But I personally understand why this talk.
2026-09-13 12:28:29
1
anathu_mpha
Mpha Anathu :
I'm here reading comments.
2026-09-14 18:14:00
0
monosile
Monosile :
Pa nkhani ya Mulungu palibe aliyense obadwa mwa munthu ali ndi nzeru koma Ambuye yekha. Chakhumi mu bible chinalembedwa ndipo ndichikhulupiliro ukamapereka chakhumi uli nfi ganizo loti ikupita kwa Mulungu nfithu zimaoindulira moyo wa uzimu koma ukakhala nfiganizo loti ukupeteka chakhumi ku moingo, nfithu ukungobetsa ndalama yako ndibwino kusapereka.
2026-09-11 02:35:30
1
user8562803966171
chimwemwe Tebulo :
unfortunately amene amayendesa chipatala ndi osiyana ndi oyendesa mpingo
2026-09-10 19:56:45
1
user9267434376163
No Nick name :
Zoona bambo anthu sakuonapo pamenepa
2026-09-10 17:58:56
1
samsonbanda302
Samson Banda :
chachikhumi ndi cha Yehova , za kayisala paseni kayisala
2026-09-11 07:00:17
1
user8013685662275
user8013685662275 :
Why the church built the hospital if the people get healed at the church? Why churches build hospital and not factories?
2026-09-12 15:09:15
0
husseinwapilomahomed
Atuweni :
You are a very intelligent person, keep on teaching us 🥰
2026-09-10 22:43:42
4
user2547810268578
NanaNa :
Brilliant question. Chilungamo chimawawa mwalankhula momveka bambo 🙏
2026-09-11 06:56:53
2
gekeba
Gekeba :
zowona zenizeni
2026-09-10 19:16:46
2
tatanowaamani
Henry :
Religion is a serious inter'l scam malume
2026-09-11 04:32:20
2
user2137887562505
Yuuki kalea :
Ndizomwe ifeso timaona kuti Chipatala chimangidwa ndi ndalama zosonkhelana mu Mpingo koma chikamangidwa palibe kuti uyu membala wathu. same with school akupangidwawa a mipingo - sikudula kwake - Kupezeka individual private school ma fees ake bolako Tiyeni ampingo yoooo. Ena mpaka kumatsekula ma business ena koma opindula ndi ampingowo ai - very bad - business yalowelera mpaka misemmpha kuiwala kutumikira ambuye kunkhoza zawo
2026-09-12 17:40:01
0
user3716958206144
KAKHWESI :
Amen amen and amen
2026-09-11 03:40:09
2
user9282618543787
Maulidi :
chalichi ndi busness
2026-09-11 07:51:39
2
user7884344185412
petros gola :
ndende ndi chi khilisitu
2026-09-12 16:49:19
1
user9267434376163
No Nick name :
It's time to wake up
2026-09-10 17:59:25
1
davidmassamba30
David Massamba :
Amen
2026-09-11 13:53:49
0
emmiemwandira6
emmie :
zoona
2026-09-11 09:41:30
0
shinobixheb30
Shinobixheb3 :
chakhumi chake anchipangila invest Kuma Business awo!
2026-09-12 06:51:12
1
masangano83
Masangano :
samasamala mulungu amapanga sa abusa ndichifukwa akayamba kumanga chalichi sichimata nga ti msikiti
2026-09-11 19:19:06
1
user9033935850369
Godfrey Chikhadwe :
komatu mwanena zoona ngakhale kudziko ukapeleka magazi,ukasowa magazi amakupatsa koma kumpingo 😭😭😭😭
2026-09-11 13:24:14
1
user8013685662275
user8013685662275 :
Christianity is a scam and church is a scam also . The church is our body and the christ is our spirit.
2026-09-12 15:03:13
0
drjay918
Snowman :
mipingo ndi business kubelana moopsezana ndi malemba
2026-09-11 08:02:44
1
To see more videos from user @alexsndergombar, please go to the Tikwm homepage.

Other Videos


About