@manupage09: #malawinewsupdates🇲🇼 #malawitiktok🇲🇼

MALAWI NEWS UPDATES
MALAWI NEWS UPDATES
Open In TikTok:
Region: ZA
Thursday 10 September 2026 10:15:02 GMT
18947
623
133
83

Music

Download

Comments

chisomokalulu167
chisomokalulu167 :
Fuso ndilakuti koma president alipo? and zikuchitikazi akuona?
2026-09-10 12:46:42
2
white.richard.mani
white Richard Maniwa :
MCP it was better than DPP because 5 years for MCP erectricity and water was not a problem
2026-09-10 16:18:04
1
sark4745
SArK :
and where are our opposition leaders ali ndwiiii akusikila ma vote apa munthu wanna zoona opanda support
2026-09-10 18:05:20
1
recksphiri
Brother Alex :
i now little by little blame my president,is quite as head of state saying nothing ngati dziko lopanda president
2026-09-10 11:20:35
25
croccodilemngona
Jahrise👊 :
Even the court has let Malawians down, how can it promote failure?
2026-09-10 11:11:39
20
user3207443453408
Ligomeka :
kod wina sangayambitse mademo please
2026-09-10 12:11:17
9
user7245317874275
louisianah :
guys dziko lonse tingokhala chete osadzuka ? zoona?
2026-09-10 11:33:52
7
assamandah
AssaMandah🇲🇼 :
Oro Kumwambako Mulungu akanena Kuti Kapito anayesetsa koma aMalawi osamva.
2026-09-10 12:10:17
1
user7062373740951
user7062373740951 :
IFE A UDF TINAKHALA TIKUKUCHEZANI A MALAWI ANZATHU KUYAMBIRA MCP ISANALOWE M'BOMA MPAKANA DPP ISANALOWE M'BOMA KUTI ZIPANI IZIZ ZONSEZI NDI ZAKUBA KOMANSO ZA TSANKHO KOMA MUDATITUKWANA KOTHERATU. ATUPELE ANAKUUZANI KUTI NKULU UJA WAKALAMBA BOMA AZIZAYENDETSA ANTHU ENA IYUJA AIZANGOGONA KOMA MUNAMUTUKWANA. ATUPELE ANANENA KUTI BOMA LA MALAWI LIKUFUNIKA OVERHAUL.KULISUNGUNULA NDIKULIYAMBIRANSO KULIMANGA POSINTH MLAMULO OY3NDETSERA DZIKO KOMANSO VUTO TILINALO LALIKULU KWAMBIRI KU MALAWI NDI MA COURT/MA JUDGE NDI ANTHU ACHINYENGO KWAMBIRI!!! IFEYO TIDZAKHALA ANTHU ATSALIRA POKHAPOKHA UDF ITADZAPATSIDWANSO MWAYI OLAMULIRA.KOMA IFE TIMAPHONYA TIKAMSANKHA ATSOGOLERI!!
2026-09-10 12:08:28
5
dalliebasi
𝐷𝑎𝑙𝑖🇱🇹 :
That's why ine sindingakhale ndi nfuti 😥 nkulu ameneuja sangathe week ine ndili ndi nfuti shuwa
2026-09-10 16:11:16
4
brighnci5nr
Bright Kaleso :
Amatumidwa ndi kupatsidwa ndalama zoyendetsela process yaku khothi kenakanso malipiro, kuphatikizanso lawyer yemwe wapereka chigamulo chonyansa chi
2026-09-10 13:16:16
1
gibys22
Gibys :
vuto lake a Malawi tinadyesedwa chipha mtima, zowona munthu akagonjese chifuniro Cha dziko la malawi
2026-09-10 11:16:26
2
julitathunga8
Juxybabie :
wachita kutumidwa amene uja komanso ma court athu honestly salikutithandiza
2026-09-10 10:33:48
5
aliebanda520
aliebanda520 :
abambo ameneaja mulungu awakanthe
2026-09-10 11:42:10
2
madalitso.mwitha
Blessings mwitha :
Powerful speaker
2026-09-10 15:25:28
1
samukwma
love who loves you🤟 :
kuyakhula kwabwino Mr 🙏🙏
2026-09-10 12:42:17
1
duncan.four20
ALFRED D.NDLOVU :
Ufiti wo koma ,mmmmmm tidakathawako ku Malawi coz the voice of the voiceless is being killed slowly slowly
2026-09-10 13:31:50
1
bernardndawala
Benzo Senior :
Well said boss
2026-09-10 10:59:23
1
feston.gwede
Feston Gwede :
kapito wakhala patriotic kwa nthawi yayitali. Uyuyu deserves respect
2026-09-10 12:03:45
6
amoschrispin
AMOS C KAFUNDA :
Malawi dziko lomvesa chisoni💔
2026-09-10 11:05:54
1
matabwamatabwa
Tengani :
Ndale mzimenezotu
2026-09-10 10:53:36
1
georgechimpeni372
Chimpeni II✨💫 :
feel sorry for my country Malawi 💔🙌
2026-09-10 10:38:39
1
prokachande
andy :
oyipa simunthu uja koma Ku DPP ndikomwe kuli ufiti
2026-09-10 11:02:16
1
raymond.kaumba
Raymond Kaumba :
Where's the president [Tears of joy]
2026-09-10 19:00:06
0
lipenga28
Olivia Lipenga :
Wachita kutumidwa amene unja aaa
2026-09-10 10:37:22
0
To see more videos from user @manupage09, please go to the Tikwm homepage.

Other Videos


About