Nditangopeza nyimbo iyi ndimkaika daily mpaka aneba anga anasamuka chifukwa dzina lawo linali Edina nde ndi ine sitimagwilizana 🥰🤣🤣🤣🤣🤣 nde ndimaiika daily kkkkk
2026-09-12 12:46:50
3
Special Owens👑 :
koma ma guy😂
2026-09-12 15:21:50
2
REIGNS🇲🇼🇿🇲 :
gailen full song Mr dj😁
2026-09-11 12:17:22
2
@black demon :
🤣🤣🤣🤣🤣 koma iwe 🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣
2026-09-11 14:46:13
2
Og drex Scott :
Koma ichi ku mixer kwanji uku😂😂😂
2026-09-11 19:37:56
3
Black Barbie🖤🖤 :
where can I find the artist ndufuna timenye corabo ndimtukwane ex wanga😂😂