I don't think anthu ama ganiza kuti kuli magetsi okwanila koma nkhani ndiyokuti nthawi ya mcp ija bwanji samazima ngati pano what's the problem
2026-09-11 22:30:30
1
Kenneth :
the important question is that why ngati speaker abwera ndi maganizo abwino nanga akumuletsa chifukwa chani?
2026-09-11 13:21:14
0
Ama jessie Bvumu :
yathera panjira sir
2026-09-11 19:12:24
0
bee chizmo,,,, :
zoona teacher
2026-09-11 17:34:33
0
MASO PA BALA :
Amwene you are going too deep. Dandaulo lilipo pano , anthu akusiyanisa chilichose ndi nthawi ya Chakwera. akuti zonsezi zinaliko better than panopo. WHY? Chachitika ndichani?
Suleman is brilliant man ☝️Vuto some government officials ndi adyera
2026-09-11 16:31:12
0
Mercy Malapa :
ambiri sitimadziwadi
2026-09-11 13:36:02
0
Chatsika De Bruyne Diness :
first comment
2026-09-11 11:08:09
0
Gracious Nkhoma :
second comment 🤣🥰
2026-09-11 11:35:53
0
John Shaibu Jnr :
Nthawi ya Kamuzu kunali paraffin anka pezeka paliponse even during Bakili time so anthu amayatsa zikolo boyi magesi anali a anthu a ndalama
2026-09-12 17:08:31
1
🇲🇼🦁 Trevor 🦁🇲🇿 :
kufufuza uku.kumayenera kudziwidwa Kaye kut kufufuza kokhako is how much you.may cost.much.pofufuza tizithu zongofunika kukonza cause kukonzako it might be cheaper