Kuteroko tikulowera kuja bukhu la Chibvumbulutso linanena kuti izafika nthawi yomwe anthu sazakhoza kugula ndi kugulitsa ngati alibe lemba ndi nambala yachilombo. Iyi ndi testing testing.
Funso langa ndiloti, Kodi UNDP ndi Malawi government ndiokonzeka bwanji kupezera azigogo athu kumudzi ma smartphone wo kuti nao athe kukhala ndi digital ID?
this is not about KUTSOGOLA,it's all about worshiping idols
2026-09-13 14:43:25
2
Martha Magwira :
Nanga kwaamene alibe 4n?
2026-09-13 08:42:25
2
Tamikamatupi :
Phone ikaonenfeka?, zikhala, bwanji
2026-09-14 02:51:38
0
jusa :
zaukape,kusiya,kukhoza,magnesium,aaaaa
2026-09-13 10:34:36
1
Meviss Tambulasi :
Munthu wa Mulungu Twaibu sananame...owerenga khala maso
2026-09-14 19:27:22
2
Cape Mobile :
Malawi government will control you better they will know how much funds you have in your bank and be prepared for MRA you will now paying tax on everything you do
2026-09-13 09:03:54
0
malombola :
love your wig dear
2026-09-13 12:51:47
1
benard k shaba :
ok zikomo kwambiri
2026-09-12 21:40:48
0
osman whiscky :
well
2026-09-13 16:29:26
0
Avide :
End time prophecy
2026-09-13 12:31:27
0
user4680041026261 :
ID silemera
2026-09-13 04:31:10
0
febembukwa :
666 ija
2026-09-13 18:17:40
0
user7466766275361 :
imeneyo ndiyezelu
2026-09-13 07:52:53
0
milly :
666 mulungu atichitire chifundo ndithu
2026-09-14 09:01:19
1
maxwelmkandawire :
that has got some missions behind My sister don't cherishing everything
2026-09-13 19:00:23
1
Dastan :
amange ma factory anthu akufuna zitchito izi ndi zankutu zongowonongela ndalama unemployment its so high
2026-09-13 14:19:29
1
kamphambe Isaac :
Much better we need more development
2026-09-13 18:52:41
1
Monsieur Nambazo :
Izi ziyenera kukwaniritsa nthawi. Zifike ndipo zayamba kale with TCM ids
2026-09-14 13:46:21
1
George Misinde :
nanga opanda. fone
2026-09-13 03:11:50
0
petros gola :
how many r u have smartphones
2026-09-22 22:46:01
0
Kingwell :
@
p
2026-09-26 08:42:13
0
To see more videos from user @alli.yusufu46, please go to the Tikwm
homepage.