Munthu akunena chilungamo ena mukuti ndi nsanje kodi sanje akapangire tonse ngati ndi bare wanthu amalawi tilibe pa bwino
2026-09-13 16:39:41
13
Sabie Izaah16 :
Ine nde ndine didimu ndikubwera nzazione ndekha😂
2026-09-14 15:53:25
7
kawina :
Anthu ambili akuku akumakhala ndi jealousy osamatero anthu akupindula kumeneko
2026-09-13 06:02:02
8
Angela Phiri :
ine ndizazionera komweko
2026-09-21 13:45:21
7
@shay :
Ndipo ndinamva kale mzanga akunena ndimayesa akunama mama zikom kwambiri bola ku Jon konkuno ndithu
2026-09-24 13:50:08
5
Tricker Mapemba Chelsea Mussa :
Inuyo tiziti transport yoti mungamabwelere sinakwane?
2026-09-14 06:04:55
6
the worshipperGetupipe Pipe :
anthu ukamawauza amati sanje oohoo ifetu timafuna kubwerera koma tilibe transport
2026-09-13 04:47:49
8
Ma Miracle :
inu musatinamize ife nde tinyamuka nthawi iliyose
2026-09-14 09:37:26
5
Brain feeder :
ndiochepa omwe amanena chilungamo big up
2026-09-24 19:40:19
5
Wachiyao 🇲🇼 :
ndipo Ku Dubai bolaso South Africa
2026-09-14 18:40:48
5
20 February 😻🦋 :
kukumvetsera with a positive mind ukunena zoona , mayiko amwenye eish sindizo
2026-09-13 15:34:34
6
Rahma's Dubai Abaayah :
nde zibwelanikotu nanga
2026-09-13 12:25:31
7
fostina kuchombe :
even ku Jon kuno Ena dzaka 8 olo kitchen alibe.nkhan ndi nzeru.inendbwera ndikufuna iPhone
2026-09-15 12:20:55
7
🅰🅻🅵🆁🅴🅳 🆂🅰🅿🅰🅽🅶🅰 :
, I know Dubai is difficult, and I understand that life here is not easy. But that doesn’t mean Dubai is worse than home for everyone. If this place was truly worse than home, I believe many people would have taken the opportunity to go back when they had the chance. But some people still choose to stay because they believe there are opportunities here.
There are even people who, when they see the police, start running because they are not ready to go back home. That alone shows that everyone has a different experience and different reasons for being here why do the run away from police instead awagwile azibwelera kumalawi or osampasa khofi supervisor akupangen terminate akupasen ticket muzibwelera.
So, I just want them not to discourage or be against another person coming to Dubai. Let people explore and experience things for themselves. What may be difficult for you might be an opportunity for someone else. Everyone deserves the chance to make their own decision and see what Dubai has to offer.
2026-09-13 18:26:30
55
honey pot 🍯 :
zikumangotengela my mum has been there for five if not 4 but she has managed to buy ten plot now she's buying a house ...
2026-09-13 10:55:29
10
Temwa Daile :
inu mubwerako lit?
2026-09-13 09:34:10
6
To see more videos from user @chimzy.timothy.gun, please go to the Tikwm
homepage.