@lhomwe_television: ankulu awa abwela ndi umbon wa ngozi ya ndege ku chikangawa eish #malawitiktok🇲🇼 #zambiatiktok🇿🇲🇿🇲 #southafricatiktok🇿🇦 #MalawiPolitics #goviral
ine l think anavara suit ya black yo anatenga chikwama yo was Rapken Abdul uja l can relate, koma awo ndi maganizo anga chabe
2026-09-16 14:36:36
3
Willard Mnyenyembe :
Chilungamo chikama lankhulidwa timati misala
2026-09-15 16:41:52
265
Chimwemwe Time :
ndizoona izi thawi ya Chakwela akanayakhula izi akanaphedwa
2026-09-15 16:49:37
82
Dziko Nkhoma :
muchedwa ndi munthu Oti mutu wake suyenda bwino
2026-09-15 17:32:27
50
chimwemwe DOZEN :
we never know he might be saying the truth and we r here busy saying mutu wake sugwira
2026-09-17 14:33:16
2
NYAKA||°2❤️🫧 :
ah iwe😂😂😂dont bring me back here plz
2026-09-15 17:07:19
47
Duncan :
Looking at the way this guy is asking his questions it seems he knows the truth and he is trying his best to hide it by confusing the guy who is explaining.