koma ine chimandikhala chovala chilichose koma chimimbacho eeeee ndipo sindiyifunayi mimba
2026-09-19 17:45:45
2
tashie 🥰🥰🥰🥰 :
Tikudikila yamimbayo please
2026-09-20 21:57:45
0
Aliana pollex :
zowoonadi
2026-09-19 13:09:30
0
nancyphiri :
Mimba yanga simava ma remedy Kaya ndipange bwa
2026-09-16 14:46:25
20
Ruth :
eeh koma ine nde sindingamalephere kukhuta chifukwa cha shape aah ngati ili yosalongosoka ndoyosalongosoka basi
2026-09-17 09:51:48
27
zaidahzaheer0 :
musatichozepo apa tangotithandizani please
2026-09-16 17:05:04
15
😍😍😍 :
meanwhile my stomach 1😂😂😂
2026-09-17 21:46:08
4
Grace Banda :
nde tiziphe🤣
2026-09-17 11:31:49
12
itz.cathie :
ine ndili nimimba koma ndikavala inuso mutha kuwasiya akazi anu zikutengera mumene ulili
2026-09-16 20:50:48
5
Faith Katopola :
Ukabereka imabwerela ukasatira malangizo ine mwana woyamba naliflat koma nachilila mpeni anadiuza kuti usakamange ikapwa chokha eee nakhalatu three months ngati woyembekezerabe after inabwerela
2026-09-17 16:35:35
3
Ednah Hannah :
😂😂😂😂😂😂 ine ikhale conchi basi
2026-09-16 14:13:38
2
Gladourcreatorhasnoracereligon :
Moti mwayamba body shaming women now,so mysogynistic zija za feeling so entitled on women's body.Osangonena ma remedywo bwanji or kuwauza azibambo okula mimba ngati ayembekezera aja bwanji.Anthutu amanenepa also because of matenda olo atatani sizingatheke and you choose to shame them.You can do better.
2026-09-17 14:03:53
8
Rabecca Gama :
Nde tiziphe aaaaaa
2026-09-18 03:59:38
1
tryness shaba :
😂😂😂😂😂😂 koma inu mwina mwaona ine😂😂😂😂😂
2026-09-17 10:05:48
0
Viola N :
remedies can work on someone pomwe wina singagwile, and some of these remedies are not safe. so let us be
2026-09-17 03:03:24
5
maria :
tiuzen changu
2026-09-16 16:17:30
5
Regina Mkweza :
Pangani changu ma remedy wo bishop
2026-09-17 08:26:43
1
Lissy🦋 :
let me follow you😁
2026-09-16 17:49:28
0
Ethel wa man city 🩵🩵🩵🩵🩵 :
koma ichi nchilungamo ndithu🤣
2026-09-17 00:53:43
0
✨💫 :
kkkkkk mwandionera kuti nanunso kundinena chonchooooo. kkkkkkk tikudya kwambiri etiii. koma ndaseka mokweza mpaka misozi kutuluka. tidikira ma remedy wo eeeeh taonjezadi
2026-09-16 18:23:38
1
EdithBless :
nenani a remedy wo
2026-09-17 05:01:41
2
keris byb1 :
Don't go through the corners talk to me directly
2026-09-17 03:41:18
0
To see more videos from user @bishophelbert, please go to the Tikwm
homepage.