@allih_5: MR EPHRAIM DUMA KUWULURA ZA IMFA YA A CHILIMA #fyp #malawitiktok🇲🇼 #100kviews #fyp #viral @allih_5

allih_5
allih_5
Open In TikTok:
Region: MW
Wednesday 16 September 2026 15:57:16 GMT
101466
3916
170
376

Music

Download

Comments

ellen.munthali6
Ellen Munthali :
Koma ine mafunso ngat awa kukhala kuti ndikunama sangachedwe kundigwira🤣🤣🤣
2026-09-17 06:08:57
14
teresabison153
Teresa Bison :
kd mesa chamba ku Malawi ndi choletsedwa
2026-09-20 08:41:24
5
thomas.masina1
Thomas Masina :
MAFUTSO ENA NDI MCP
2026-09-19 12:12:18
4
praisegwireni
Praise Gwireni :
mulungu ndamene akudziwa munthu singamukhulupiler
2026-09-16 19:03:59
10
mervisnambayankaw
Mervis Nambaya nkawombe :
Koma anthu munawona zithu
2026-09-16 17:33:22
10
violastacy
Nancy :
we joke too much😂😂
2026-09-16 19:57:10
9
blessingsgondwe42
Blessings Gondwe :
nde mesa amati ndege samayionesesa kamba ka weather kkk so anawaona bwanji a chilima
2026-09-22 09:27:09
1
user7592584578034
Felix pentani :
ameneyu mbwelela zimenezi ndi amene anapha achilima ndi anthu ena aja
2026-09-16 18:11:55
2
wezieedson
WEZIE EDSON :
Mmmmmm nkhani iyi yipitilile ndichilungamo aaaaa
2026-09-26 20:38:03
1
kukwenda56
kumwenda :
ndichifukwa amakana kuona nkhope
2026-09-16 17:48:34
8
priyangoni
PRIYA NGONI 💞✨💝 :
😂😂😂 koma ambuye zili pas pano
2026-09-17 14:36:09
1
michael.phiri5
Michael phiri :
ku Malawi aaaa ndi dziko pa lokha
2026-09-19 18:53:50
0
alinafemuthina
alinafemuthina :
A Chilima timawaziwa indeed,, bamboyu muli chi confidence,,
2026-09-23 14:01:50
1
rateefah.samuel
Khadija❤️ :
Ifeyo with who ???
2026-09-16 18:25:46
2
jacobmzumala511
Jacob chingaipe :
god bless you
2026-09-16 17:59:37
1
lone.wolf.1975
Lone Wolf 1975 :
I'm not buying his words,sizikumveka bwino.
2026-09-16 19:26:08
3
ken.simsokwe
Ken Simsokwe :
koma umphawi ndimatenda kaya
2026-09-16 18:12:56
4
lommietembo
Lommie Tembo😇😍 :
follow
2026-09-23 17:21:16
1
peoples.voice.1
PEOPLES VOICE PARTY :
nfuti ikuyenera ndithu iyesedwe pa iwo as part of inquiry confirmation kkk
2026-09-17 07:33:15
6
ethelthobowa3
Ethel Thobowa :
padziko lapansi palibe chisinsi mulungu alipo ndthu 🙏🙏🙏
2026-09-19 03:31:46
1
stefanodaudi188
africa :
Kodi mafunsowa mukufunsa bwanji
2026-09-17 12:41:50
2
umelusimumba
Melusi wa Flo💞 :
chilungamo ambuye mkuchiziwa cha Ngozi
2026-09-16 18:29:39
2
queengopani7
Queen Gopani :
active
2026-09-16 19:40:05
1
selefie.jackson
Selefie Jackson :
atiwuzeni.bwino
2026-09-16 18:55:33
1
olivia.zimba0
Oli coringz :
mzimu wawo sir chilima uziusabe muntendere
2026-09-17 16:53:33
1
To see more videos from user @allih_5, please go to the Tikwm homepage.

Other Videos


About