@jumamasacheabdul: nkhani ya Chipewa pa Swalah tacheza ndi Mufti Muhammad Jaliya Deya kufotokoza mwamvemvemve!!

Juma Abdullah Masache
Juma Abdullah Masache
Open In TikTok:
Region: MW
Friday 18 September 2026 13:44:00 GMT
30535
1114
165
158

Music

Download

Comments

ismaelkalulu
Ismael kalulu :
akut zinayamba ndi abu hanif zosavala chisot patapita zaka 180 nde akutinso swala yafardh ndiyofunika chisot koma hajj ili ndi lamulo losavala chisot komanso kumeta mpala nde zikufunika kuwapeza sheikh wa ndimabukhu ndikuunikirana nao mwina nkutheka sheikh wa anawelenga mabukhu ochepa ena awerenga mubukhu ambiri please kawunikiren amene mwaphunzira kwambr
2026-09-22 06:09:43
0
abdul39854
Abdul :
Sheikh ine ndili ndifutso kodi zoyimba zija zilinso mu Deen momwemo nankha ndi Hadith yanji ya nyimbo popeza ambiri ife takuziwani chifukwa cha nyimbo?
2026-09-22 19:39:58
0
presnelraj1
RAJ ®✨ :
kulowa ku moto chifukwa chachisoti chisilamu sichovuta chonchi Anthu please 🥺 musamapange zmenez aaaaa
2026-09-21 20:33:48
0
user6145213109951
Ruckshan Benson :
Kodi hadith yo ili mu buku iti kapena imam ndan kwa ma imamu onse amene alipo anali mayo kapena hadith yo ili pa page yanji kapena number chan? Tiuzen please chifukwa ine ndafufuuza zoti popanda chisoti ukalowa kumoto kapena chisoti ndi faradhwi or masuhaba tipaseni. Kodi onse amene amaswali ku hajj aja samalowa munzikiti? Koma bwanji amavula zisoti nkumati imeneyi ndi nyumba ya Allah. Plz osachipekela chislam bodza. Plz
2026-09-20 18:40:53
2
assalaf23
assalafiyyah :
nganga bodza silabwino koma hadith mumaiziwa
2026-09-18 19:57:43
3
twalha.friday.sula
Twalha Friday sulaimana :
Masha Allah auzen anyamata Alero omwe akumapita kumadinah kukaphuzila mwano osati deen
2026-09-19 08:09:49
2
fahadi.amish
Fahadi Hamidu لقمان :
Petani sheakh ku hajj muoawone kumeka
2026-09-18 17:42:32
3
haffeez.kazembe
طيب عيس :
سبحان الله koma ma hadith ake wodwala dwala
2026-09-19 20:31:59
1
suraq38
SURAQ🕋🕋🕌🕋 :
taponyan Nambala ya asing'angawo
2026-09-19 15:10:29
1
yakinimw0
Yakinimw :
perfect naaaaaam 100 percent
2026-09-18 18:51:26
3
abdulraheemwasili
Bøî słëñdær💦 :
22 wake uti
2026-09-18 19:43:12
2
shalifu.kabati
SHALIFU KABATI :
uyu ndi dolo
2026-09-19 10:53:33
1
njuchivaxytkorkac
ekwendeni vibes :
Hadith number yanji?
2026-09-18 18:49:01
1
fridayjalali
bwana mafa :
Sunnah
2026-09-19 09:12:39
2
ishumael.martin172
ishumael Martin :
22A ndikuwaziwadi sheikh wa
2026-09-19 20:41:41
0
user2748229308235
DJ SILAFA BOY GOBALIRO SIR :
Naam she
2026-09-21 00:07:10
1
mmaira42
Mmaira :
aaaa
2026-09-18 20:39:13
0
hope.foundation.ma
HOPE FOUNDATION (MALAWI) :
ndiye amat عن أبو هريرة kkkkkk عن أبي هريرة
2026-09-19 05:37:00
0
mchochoma.g
Mchochoma G :
Naam sheikh 🙏
2026-09-19 13:55:56
1
ridhwanarckilu
Abou Yazeed :
Sheikh mbuli
2026-09-18 20:23:12
2
chisomobello4554
chisomobello4554 :
ameen
2026-09-19 12:08:01
1
innocent.yassin7
Rill G 1 :
kkkk koma nshito ilipo
2026-09-19 04:33:14
1
uthumanaidin
NASALA :
zaziiiiii
2026-09-18 21:28:07
1
user5621120283172
mwamadi :
active
2026-09-18 19:57:05
2
To see more videos from user @jumamasacheabdul, please go to the Tikwm homepage.

Other Videos


About