Kodi paja ankayendtsa ndiyetu eeeti? Inquiry iyi yalepheraso kumutchula ngati mmene agalu amayembekezera chifukwa mboni tu ngakhale zinakochedwa koma zikutitu ndege I agwa.
2026-09-18 20:10:17
2
mmbulujr :
no we need to cancel that holiday
2026-09-19 04:53:49
1
Mphatso Damba :
Wainyuma wainyuma
2026-09-18 19:05:15
2
John Drillz :
Asatuluke ameneyo
2026-09-19 05:41:46
2
Let love lead :
Palibe kuthawa apa
2026-09-18 19:38:38
1
Brenda Mando phiri💝 :
zaziii
2026-09-19 07:11:18
1
Felix Mponda :
athawa chani
2026-09-19 03:10:30
1
Monosile :
akawonjole misampha yazachuma yomwe mwana wake adacheta asadachoke mboma, Yendani bwino koma ma surveillance cameras akulondilani zonse muzichita kumangalande tiziziona kuno kumudzi