jacket mwavalayo ndi Tie yo munapanga ndiinuyo? Anthu akuda ankavala ma jekete? if you apply same logic on everything around you you will be traumatized
2026-10-15 09:35:55
0
Rashy🥂🍾🍷 :
ndpo ndfe athu omvesa chison😅
2026-10-17 06:40:23
0
Mlowoka Chirwa :
anthu oganiza chonchi tilipo ochepa Mmalawi muno
2026-09-27 09:15:01
11
scoccoh :
koma apa ndiye mwandiyakhulila bwino
2026-09-20 10:50:14
7
NYAMALABWE :
Ambuye Yesu khristu ndi njira chowonadi ndi moyo ,opanda Yesu khristu sazapeza moyo.mlandireni Ambuye Yesu lero
very very true , Mulengi ndi mmodzi koma zipembedzo zosiyana , Pali chinachake chinalalkwikad ndipo nchifukwa chake kukangana sikumatha chifukwa zipembedzo zi sizathu.
2026-09-25 16:41:12
1
alinafetrywel :
Pamenepo, pofunika kufufuza ndithu
2026-10-04 13:15:42
1
sellinah :
Ndizomvetsa chisoni kwambiri
2026-09-20 10:22:54
3
chikumbutso mankhwala :
ndikubwera komko ambuye apa mwamasura chilungamo
2026-09-20 20:10:08
1
Wisdom Nqumayo :
Akulu tikumaneko i wanna hav peope like u around my table! PALICHINA CHAKE CHINALAKWIKADI
2026-10-04 09:59:55
2
jereka :
Funso labwino
2026-09-20 11:21:02
2
SHERRY NAILS :
Tili limodzi
2026-10-04 18:20:12
0
Gofine :
wise Dem up
2026-09-20 16:34:30
1
Niger^ :
uyuyu ali out of matrix
akulankhula truth🔥
2026-10-10 20:55:25
0
NYAMALABWE :
kabatizeni anthu amitundu yonse padziko lapansi.dzina la Atate ,Mwana ndi Mzimu oyera.
aluya, amitundu tonse tidapulumutsidwa mwa Ambuye Yesu khristu.
2026-09-27 18:21:46
0
Andy cee 3 :
Aaaaa
2026-10-16 18:11:05
0
Pique mw :
I just love the way you are digesting it ..we are really working up .we need more answers to such kind of questions
2026-10-04 20:37:46
0
Collings :
who is this one ndimupange follow
2026-09-20 12:03:58
4
mikebramera :
kugolakwa otsaziwa malemba
2026-09-20 21:42:42
1
MAWULIDI :
chikuvuta ndi ukapolo wa mmaganizo
ukapolo unabwela ndi zipembembezo
kutha kwa ukapolo zipembezo zobwela
zakakamila mmaganizo pakufunika anthu ngati inu ndi ine omaganiza kuti chinalakwika ndi chani ndikupanga chiganizo chobwelela ku chikuda
2026-09-20 12:04:53
3
Zgavy Diel :
apa ndie mukundichitira chifuniro changa,tauuzeni ntundu wanuwu baba eee chooonde tazipulumutseni zitsiru zinazi.ndie amachita makani ati chifukwa awerengetsetsa
2026-09-20 14:40:50
1
HowardM Banda :
koditu scam yawo iyi ambiri tikuyitiluka
2026-10-16 03:00:58
0
To see more videos from user @khristjah, please go to the Tikwm
homepage.