sherkh sudziwa chimene ukulankhula uchimo umakhala mumtima mwamunthu chimene ukuganiza iwe sizimene ndikuganizo ine for example abel ndi Kayne anali ana amunthu modzi koma anali osiyana maganizo so ubatizo ndiwoyenelela
2026-09-21 03:46:08
0
keyita yassin :
sherkh kuyakhulamoveka bwino osava sava wakuva wava
2026-09-21 01:34:33
1
Misheck Junuary :
Program iyi igothesedwa asilam samadziwa kuti yes u ndi ndani awo akungotsusa zinthu zoti sakudzidziwa adzikachita ku chisilam kwaoko baci
2026-09-21 06:57:38
0
CHITSOKONEZO 🐇 :
akhristu koma kupopana ndi kukakamiza zithu 🤣🤣amagova koma zamavesesa pali aire apa ubulutu choliga wina akhale mulugu bc koma ali muthu 🤣
2026-09-21 10:23:00
0
To see more videos from user @user8169415761687, please go to the Tikwm
homepage.