ambuye muwapase athu akufa chiusilo chosatha ndipo kuwala kosatha kuwalise maso awo ause ndi mtendele amen 😭😭😭😭😭😭
2026-09-22 19:11:45
1
janet :
ndimangokumbukila tsiku la mother's day anandisiya ndili ndi zakaz 6
2026-09-22 19:26:50
1
mery mdokhwe :
continue rest in peace amayi anga 😭😭😭😭😭😭😭😭😭
2026-09-22 14:45:32
1
DJ SAM PANGOLIN :
bolani inu mwapangako ma mother's day angapo ife palibe oloko imozi anatisiya tili ana sanadye anango vutika ndi ubeleki owawa uja limbani mtima ndipo ambuye oziwa kutothoza akukuteni ndi mtima wachili mbikiso
2026-09-22 04:28:16
13
Lisha :
nyimbo imeney imandlilisa abale 😢😭😭
2026-09-22 12:50:33
2
Thando :
i lost mine too 2022,zimandivuta kulimba mtima mpaka pano n deep down i hate mother's day,ambuye muwapatse anthu akufa chiusilo chosatha ndiso kuwala kosatha kuwalise maso awo ause ndi mtendere..Amen
2026-09-22 08:15:13
6
Susan :
eish pepani kwambiri mama
2026-09-22 19:16:54
1
Precious D Tipembe :
Pepani chemwali,,, Mulungu akutonthozeni🙏🙏
2026-09-22 19:05:19
1
Christina Madengu :
mwandikumbutsa nane anandisiya ndi zaka7
2026-09-22 17:49:17
1
thandie :
sorry mam mmmm ndarira mmmmmm 😭😭😭😭😭
2026-09-22 12:56:34
1
Do...e 🦋 :
sorry dear 😞 😢
2026-09-22 14:43:46
1
Towera Chikwati :
Sorry imfa kuwawa 😭😭😭😭😭
2026-09-22 10:53:32
1
muhammaddi. sayidi :
zosayeta asisi😭😭😭😭😭
2026-09-22 13:38:10
1
Tiya :
Sorry
2026-09-22 20:50:26
1
Gezina Chauwah :
Sorry 😭😭😭
2026-09-22 18:20:27
1
lister :
sorry for loss dear
2026-09-22 09:45:57
1
Roshany :
pepan.. mulungu apase moyo wautali mayanga
2026-09-22 16:23:11
1
Caleb :
pano nnalimba mtima ine mayanga anazumzika azipuma😭😭😭
2026-09-22 17:57:01
1
Martha samison. 💗 :
sry Mamie tikachita bwino tizakumana nawo
2026-09-22 15:30:20
1
Tiyamike Joseph c :
sorry ine mom anapita pena ngati ndikulota amama ndimakonda kulibe
2026-09-22 15:22:06
1
hallimamagombo :
zosayendatu mmm mbale pepa ine pano adandisiya ndili wachichepere mmoti mawasowa tsiku ndi tsiku @
2026-09-22 11:53:16
1
Madalo :
Ine Mai komaso bambo anga onse sinkuwadziwa moti ngati ndaonako kholo ndi agogo koma imfa yatengaso 😭😭😭😭💔
2026-09-22 12:30:25
2
To see more videos from user @user9981470637215, please go to the Tikwm
homepage.