Sanamutemberere but the moment he spoke back death was reversed back to sender he declared life in his life and God granted it so we just have to be careful what we wish for our nebours.
2026-09-22 10:40:26
81
Malige Bandah :
sanatemberere koma okumba dzenje amagweramo yekha eetu tizisamala mayankhulidwee
2026-09-22 12:24:08
9
Cool96🦋 :
kodi when was this mhu
long live apm
mpaka he pleaded ( don't wish me dead)
SAD
2026-09-22 10:02:30
45
HBmaterial :
Kodi mawa uziliopa chifukwa chani?
2026-09-22 10:43:03
15
OLIVIA MEDIA :
izi zinalidi zochokera pasi pa mtima 😔
2026-09-22 08:54:06
28
Nessa☯️🫶🏽⚖️🖤🤍 :
Sanamutembelele nahh…. But omukumbira zake zenje amagwerAmo yenkha… athu amatha kumamuikilia muthu malile… he spoke the truth and it’s sad that the ones we thought ndiokhalitsa anatsogola.. osamamufunila muthu zoooipa
2026-09-22 10:05:16
36
Easter Gondwe :
Mau awa amandikhudza
2026-09-22 12:12:43
8
Mariam Kachale :
amene muzimunyozabe petar munthalika muzikumbukila mawu amenewo
2026-09-22 12:33:03
3
SteveDem :
APM sakonda kuyankhula kwambiri koma ngati zinafika apa mudziwe anakhudzika kwambiri [Crying]