@james.maliwongo:

James Maliwongo
James Maliwongo
Open In TikTok:
Region: MW
Tuesday 22 September 2026 11:40:18 GMT
20418
435
245
80

Music

Download

Comments

ruth.chatha03
Ruth Chatha :
ndipo alindisoka uyu safa koma angoziwa kt ambuye inuyo mulupo😭😭😭😭😭😭
2026-09-23 08:09:46
2
adam.maundala4
Adam Maundala :
Guys kod dzikol likupita kut?
2026-09-23 07:58:32
0
mangadzifanny
mangadzifanny :
mulungu siomuseweretsa tiyeni zina tizicheza koma mulungu ndiye tisamapangenaye phada
2026-09-23 09:52:08
1
robertkankhande72
robertkankhande72 :
Uyutu sakufa koma Mulungu amuchitila chinthu kuti aziwe kuti Mulungu aliko ndipo azalankhula ndipakamwa pake
2026-09-23 07:39:29
2
samzy833
Samzy :
Nthawi yatha ndithu tisamalise, Chifukwa oipayo awoneka ngati munthu, Ambuye atiyendele😭
2026-09-23 16:17:07
2
buhari2446
buhari🇲🇼 :
cool am waiting for results after few minutes later
2026-09-23 12:49:12
2
ghatto.kennedy
Ghatto Kennedy :
ada awawa ndiwanzeru guys tampangeni understand there is knowledge
2026-09-23 01:17:13
11
felix.chalela
Felix chalela💯 :
udolo sitipanga padzina lamulungu ehe 💔
2026-09-23 04:46:07
2
user403348306013
constance :
mulungu akuoneseni chizindikilo kuti alipo
2026-09-23 11:39:38
1
.damz.dinky
Damz Dinky :
otembeleledwa
2026-09-24 15:53:45
1
clement.chunga8
clement chunga :
mulungu akukhululukire
2026-09-23 04:34:04
2
chileka.boys
Chileka boys :
mulungu alipo ife tikamupempha amatipatsa
2026-09-23 07:40:03
2
chizeeyakudah
Chi zee Yakudah :
Location please munthu onyoza mulungu inuo kumangomuyang'ana alomwe akt inuo osamugenda bwanji olo kungomuotcha bas
2026-09-23 05:12:52
2
focus9922
FOCUS🍫 :
I THINK HE HAS SENSE
2026-09-23 05:07:46
4
tella67a
TEllA :
facts
2026-09-23 15:33:42
0
klaustfx
Klaus FX :
this guy he's awakening he knows what he say zipembezo zimuopsezan ndipo ndizomwe zimakupangani athu kukhala osaukitsitsa kwambili because you always kuopa mulungu pamene mulungu sioyenela kuopedwa this guy has a key to escape from the metrics musamuopseze munthu wapanga ma ganizo ake musiyen mulungu wanuyo amuweluze yekha
2026-09-23 05:30:47
0
mphatso567
Esther :
ayi zikomo mulungu athale ndichifondo
2026-09-23 06:04:38
1
user5336743305968
Gega Gega :
kkkkkkkkk kkkkkkkkk kkkkkkkkkk koma guys osati mundimenyethu ai kkkkkkkkkk
2026-09-23 10:38:23
1
chippewa350
CHIPPEWA :
Adah awawa ndamzelu kwambili ndikugwilizananawo, mulungu kulibeko and anthu ali busy kuteteza mulungu mmalo mot mulungu ateteze anthu
2026-09-23 23:03:47
1
jonesiwaansimamkw0
Jonesi Wa Ansima Mkwamba :
mmmmmm mulungu akukhululukilen wallah mpaka kulimba mtima kt mulungu kulibe ayi zkm
2026-09-23 07:05:18
2
chiwunjiza1719409601932
chiwunjiza chiyenda :
ulinisoka
2026-09-23 04:41:07
1
haroldnyimbo
haroldnyimbo :
Aliyense ali ndi zikhulupiriro zake,musiyeni munthu ndi chikhulupiliro chake inu ndine ngati timakhulupilira Mulungu zikhale choncho.Musamunyoze munthu kuti watukwana Mulungu wakuuzani kuti kulibe pa chikhulupiliro chake
2026-09-23 17:59:28
1
kakosamulenga
kakosamulenga :
masewera kumapanga koma osati ndi Mulungu
2026-09-23 04:33:54
2
user8446136750444
Jay_N :
This brother we are vibrating at the same frequency
2026-09-23 08:43:54
1
stanly.makolija
Stanly Makolija :
Kuluyi ndiwamisara kd asamasewere ndi mwini moyo ay
2026-09-23 03:50:40
1
To see more videos from user @james.maliwongo, please go to the Tikwm homepage.

Other Videos


About