no comment,,, Mulungu samaona gender,,,we are all the same in the sight of God
2026-09-23 19:58:08
0
Justin peter :
izitu ndizoonadi
2026-09-24 04:50:09
2
chisomo :
Amen amen amen!!!!
2026-09-23 20:07:33
2
user2861778176002 :
chiphuziso chopusa, ndife ofanana pa maso a mulungu chifukwa chake yesu khristu anayikidwa mwa mayi maliya, kumeneko ndikuweluza musayiware kuti muzaweluzidwa osanamiza anthu ulaliki wanu ndi iwaboza
2026-09-23 21:18:34
0
EGC :
Uthenga opanda chigamba uwu amen asogoleli in addition mulungu analenga munthu nampangila othandizila wake chifukwa munthu you samkasangalala payekha and othandizilayi anachoka ku nthiti ya munthu ndipo ya kumanzeleko pomwe munthu anachoka kudothi ichitu chilungamo
2026-09-24 04:20:31
1
Joycooking&lifestyle :
Aaaa aaa
2026-10-24 14:02:18
0
shadreckfilimonmasina :
oipa adziweruze yekha
2026-09-24 11:25:18
1
elsonpitani :
amen and amen
2026-09-24 08:54:26
2
Fountain :
No comment ndingachimwe koma sinaulandire uthenga uyu.