@legendary265studios: It’s a what azimayi ? 😂😂 MC ndi Mai Gondwe omwewa 🔥🔥🔥

Legendary265 Studios
Legendary265 Studios
Open In TikTok:
Region: MW
Friday 25 September 2026 07:12:29 GMT
275617
12443
795
2671

Music

Download

Comments

juliet91071
juliet91 :
zaboza zimemezo ukakwiya paliponse pamakwiya,ma feeling amachokera muntima kuvaya kuubongo,oloko zibambo akakwiya Malo ajaso samapanga respond,nkhani mdiyokuti musamakwiisane mpaka kukagona mutakwiisana sizabwino ayi,pezani nthawi yokambilana nkugonjelana kukhululukirana,osamakagona muli okwiya ma feeling amathawa,
2026-09-25 11:27:08
214
wongie07
Wongie :
we are under 18 guys
2026-09-25 10:16:14
56
user7834108151244
ZA PHINDU ❤️🔐 :
Sibasi apapa Shawa yanga yachitika kale....nanga chatsala kuti ndinve nchani??😂😂
2026-09-25 10:36:36
265
user8256704690337
user8256704690337 :
achina mercy tilipo???
2026-09-27 06:22:14
2
mimibeib3
michelle chilanga2 :
munthu ndakwiya ndikwelana naye bwanji hiyaaa sipanga ngt sikufuna hiya
2026-09-27 13:18:51
2
lusekero8
Lusekero❣️ :
munthu wamupeza nd ma message a chibwez uyambira pati😂😂🤣
2026-09-25 13:12:46
90
omalicha19766
omalicha19766 :
za ziii
2026-09-25 11:22:11
61
user23945599863658
austin :
Basi nkhani daily izingokhala zonyengana
2026-09-25 10:20:43
56
user284679867320
Ronex fabiano :
izizi amalankhula Mai ndi bambo ako Ali pomwepo??
2026-09-27 10:05:06
1
user4269753301611
CHARLIE :
z that pa square @ Zomba campus Malawi College of Health sciences ??
2026-09-27 14:47:30
0
famo265
We are famous🌍🔥🥹 :
Izizi nane azandiyakhula mayanga ndi bambo anga akunva ?
2026-09-26 14:44:43
0
usercha118
Charie🥰 :
izi amaankhula mai ndi bambo ako alipompo? kkkk
2026-09-25 09:48:04
30
shyn672
nazulu zulu :
I will use the advice kukayendetsera chibwezi changa
2026-09-25 12:56:05
23
tashamaephiri
Tasha Phiri :
mai Gondwe to the world 🥳🥳🥳
2026-09-25 10:26:02
1
265mm0
Memoi :
Mai Gondwe amayithaaaa
2026-09-25 17:07:00
0
prettyghettothing_
Emma Sangala :
Za ziii oh my goodness
2026-09-25 21:54:07
10
cutiewifey1
cutie wifey🥰💞 :
koma kubanja kuli zochita zambiri eeeeh 😂😂😂😂 the way makwiira ine wallah chilichonse Paine chimakwiya
2026-09-25 18:55:55
21
idrissadaudi650
Idrissa Daudi :
ndikanakonda nkanamawonela this vidio ndi nkaziwanga koma ali kumudzi ndingatani kuti azaionele nawo
2026-09-27 02:06:40
1
thyela.simba
thyela.simba :
Mwalangiza tonse
2026-09-25 09:42:36
35
mercie1204
mercie1204 :
Tsono Dzina langa layamba kufanana ndi doyoyo
2026-09-25 11:42:36
10
christinabeseni
christinabeseni :
Zimatheka if u are happy
2026-09-25 09:23:16
17
esnellyngoma965
sochilibwa :
munthu wafika 6am chipitileni dzulo kumowa, basi uzimpatsa zoona izi?
2026-09-25 16:07:51
13
drharryphiri
Dr Harry Phiri :
she needs to be protected
2026-09-25 11:09:16
6
chachayasi2
chacha yasinta :
ambirife ma bridal shower tapanga kale angosala ndiaku chimunao
2026-09-25 10:46:42
13
user5668415929319
thaateez :
ngati nkhani yake ndiyomweyo am going not🤣🤣🤣
2026-09-25 09:39:21
8
To see more videos from user @legendary265studios, please go to the Tikwm homepage.

Other Videos


About