@alisu557:

Rasuru.  +27817434345
Rasuru. +27817434345
Open In TikTok:
Region: ZA
Friday 25 September 2026 08:40:51 GMT
151843
6112
418
423

Music

Download

Comments

ndabonella
ndabonella :
chonena ndilibe but my late mom once said Mcp ís evil
2026-09-25 10:26:32
142
akumudzi4
DYOMBA 5 :
izi apanga ndi a DPP popereka ndalama ku TNM kuti aipitse mbiri ya MCP.
2026-09-25 10:25:48
31
sallymusicmusic
sallymusic :
plus umbuli osadziwa kuti they'll see more than the numbers
2026-10-05 06:02:07
0
successmamie2
Mama Success :
koma funso ndilakuti ngozi ya mtundu wanji yowasiya anthu ndimapant okha?
2026-09-25 18:44:59
30
tracybakaya5
Tracybakaya@gmail :
Apapa ndipomwe tingavomereze mawu abambo msusa kuti Mulungu wachikangawa anaona chilichonse
2026-09-25 12:46:50
55
shafinacassim
Shafina Cassim :
follow
2026-10-04 18:46:15
0
patricia.gwedemul
Patricia Gwedemula :
Eish ndykt anthu aja anachitadi kuphedwatu eti?
2026-09-25 17:49:42
19
thebestcellphoneclinic
GSM-1TOUCH BEST PHONE REPAIR :
mcp will never come again
2026-09-25 16:17:45
21
user45148174374120
Jambo Chilinkhanda :
sindikuona coment olo imodzi ya mcp tu apa alikuti masupporter a mcp kodi?
2026-09-26 00:31:11
9
eddah.nyambi
Eddah Nyambi :
chilima ankapemphela ndithu
2026-09-25 13:36:39
19
thembi35013
Thembi350 :
mulungu anatibisira mawa 😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭
2026-09-25 09:20:09
30
croccodilemngona
Jahrise👊 :
Wamisala azaoneka inquiry ikatha!
2026-09-25 11:06:34
12
user71037968447211
BKF :
MCP never again
2026-09-25 11:33:11
17
janetpachanya
janet pachanya :
apapatu zuchita kuonesa kuti ndare ndi ufiti
2026-09-25 15:12:36
13
sibongire0
sibonyande :
😢😢😢😢😢😢 yogwila corona yija nde yimachita kuonesa kuti anali ndi moyo after the crash
2026-09-25 12:41:44
29
mcherophwanya
Ryash Financials :
koma MCP mtendere simudzaupeza agalu inu
2026-09-26 04:00:07
10
yemi924
yemi :
ifa inandiwawa iyi😭😭😭😭😭😭😭
2026-09-25 13:22:52
15
user8461997132811
Elias :
Ndakhala ndikunena ine kuti mcp payokha siingaloweso mmboma ngakhale zitavuta bwanji
2026-09-25 20:22:43
8
mauza7426
mauza74 :
inavuta ndi agreement ya 5 years aliyense, wina anamva kukoma u president
2026-09-25 16:51:30
7
lonjezomahata
Lonjezo mahata :
MCP yakupha sazabwereraso amewo never
2026-09-25 09:51:19
5
ismael.salsabeel
ISMAEL SALSABEEL :
Ndi Mthawi yomwe MCP imanyonga anthu athu aja, MCP never again
2026-09-25 09:26:32
8
mcnevermauwa145
Mcnever Mauwa :
Yakwiya ndi mizimu bas mcp never
2026-09-25 09:25:23
6
luciosduncan.gmail.com
John Duncan :
ijayi inali well planned mission thats why a MCP samafuna kunva nkhani zimenez
2026-09-25 13:29:46
6
auntyauntyaunty4
Takondwa Mbewe :
zikoli mwini wake ndi mulungu zobisika zizaululika[Crying][Crying][Crying][Crying] kwamulungu kukakhala ntchito
2026-09-25 11:36:23
5
abanda071
Oxygen :
ndi iweyo ukuuza ndan
2026-09-29 03:47:45
0
To see more videos from user @alisu557, please go to the Tikwm homepage.

Other Videos


About