ine nde m'dami wanga anali nzanga weni weni pamaso ngati amandikonda koma kumbari akundinyoza mpaka kundithesela mamuna yemwe timayenela kukwatilana zoti sindivesa mpaka lero
2026-09-25 22:43:44
4
Sosten S Banda :
yes uve iwe mzanga unandithetsera tchito kusukulu kuja ndinali koma lero undiwone kumwamba kuli Mulungu
2026-09-26 03:09:54
1
Eliza :
Mulungu atitalikitse kwa anthu amenewa
2026-09-25 17:47:32
1
Amunanga :
ndithudi ineso panopo ndikungolila tsikulililose chifukwa chazanga ndinalindimimba koma inachoka mosayembekezera koma zapezeka kuti zangayo anamuwuza mamuna wanga kuti ndachita kutaya mimbayo mamunawanga anazivera zimenezo panopo mamuna wanga anasitha zoyalhula ine sizikuveka ndenditani ine chifukwa ndimamukinda kwambili