@realtalkmphatso21: #angelanwosu

mphatso🇲🇼🧚
mphatso🇲🇼🧚
Open In TikTok:
Region: MW
Friday 25 September 2026 17:13:13 GMT
193674
9582
497
304

Music

Download

Comments

asiyatu122
Asiyatu :
ineyo sindingachite amuna alero ayi bola ndipereke Kwa ana amasiye
2026-09-26 09:04:59
58
umiwangu
Umiwangu :
ineyo chili chonse chomwe chandiwandikira ndimamugulira ngati mamuna wanga koma tikayambana ndamuwuza zanga abweze
2026-09-25 20:39:31
20
user8409036681995
Lindi'sThrift💅👚 :
Amuna ake si aku Malawi 😂
2026-09-26 08:39:19
24
1986julian
Juliana Suit :
Amuna ake mahulewa ndikawononge ndalama zana mpake ine ndilibe ndalama sure
2026-09-27 11:32:15
9
luciadama05
luciadama302 :
uli ngati ine mum inenso ndimamva bwino ndikamapangira zabwino mamuna wanga
2026-09-25 18:11:00
17
user993140724
William :
My wife can do that despite everything
2026-09-26 12:22:07
6
neliagoliyatimila
neliagoliyatimila :
bolani ndipase achimwene anga sindi ngapange
2026-09-29 12:40:13
3
beatphonela
beatphonela :
ine or ndasi sindinganyemere
2026-09-26 13:48:24
8
atupere.kayingah1
tupe Baby :
ziwanda zilindi ex wanga singachite ngat ndimagulila zovala kenako kuzandi sithila nde galimoto angafike pati 🤣🤣🤣🤣
2026-09-29 17:06:30
1
hezel581
Hezel :
anachita bwino azikakwelamo ndi anzake
2026-09-28 13:35:47
1
cathyjambani
cathy🌸🌸 :
masewela awa ine ai bola mkapase brother wanga andiyamika osat agaluwa ainakewa
2026-10-02 21:40:21
0
catherinechimbaza2
Catherine :
ine anthu awawa amandiwaza saname🥰🥰🥰
2026-09-25 17:27:50
17
marthankhono
Martha Nkhono :
ine singachite
2026-09-26 04:45:18
1
happie2712
nachibedwa :
vuto ndiumphawi koma tikanapanga
2026-09-25 19:15:06
8
nelichapatuka302
Nellie chapatuka :
ambuye ndidaliseni ine amunanga ndizazizimuse eeee ntchito akuyigwila
2026-09-26 12:44:55
2
patriciamilli871
Patricia Milli1234 :
ine sindingapange zopusa kutenga chithu kumupasa mamuna agalu amenewa samayamika ine or chigumu sindingagule😅
2026-10-02 10:16:53
0
hanisha545
Hanisha Li :
Ine sindingachite Bola ndikaike ku bank😂😂😂😂 mwina Poti ndine ochepekera Koma momwe ndimakondela Ndalama ndikamugulirenso Ine.
2026-09-25 20:55:24
1
user307429578245367
user307429578245367 :
koma mulungu angondidalisa ine ndimasilila ine mtampangila mamuna wanga izi
2026-09-25 19:16:10
5
mirrambanda
mirrambanda :
singachite nachitapo ine kusakila ntchito boyfriend wanga kumafola ndalama zambiri akuseweza ananichinjila nzeru mamuna ine amuna mmmmmm🙌🙌
2026-09-30 18:24:26
1
user27810086868202
Mirriam :
ine olo sweet wandodo wa R1 ndimathokoza😂😂😂😂
2026-09-26 20:44:14
1
jenipher.makasu
Jenipher Makasu :
Ena ati sangachite Azimayi mwamuna akamakupanga support mu zinthu zambiri kukulemekeza kumakupasa zosowa zako .Mtima okha umakuwuza kuti panga izi .
2026-09-30 16:05:30
2
user6051900036110
maria💞💞💟 :
vuto ndindaram km amuna anga ndikanawagurira
2026-09-28 11:00:38
1
rabsonchikondi
Bless :
100,000,000 that car mukanapanga check bwino mtengo wake
2026-09-26 17:25:16
0
sibo4019551596300
sibo nyirenda :
ambuye ndipasen chuma ine naneso nzawa gulire galimoto amunanga☺️or njinga yakapalasay nzawagulire
2026-10-03 16:24:57
1
ishutonex
Ishu Tonex :
yachepa 100,000,000 million Malawi kwacha for that machine
2026-09-26 13:06:06
4
To see more videos from user @realtalkmphatso21, please go to the Tikwm homepage.

Other Videos


About