@ispeaklearningplatform: Inuso muntha kuphuzila English or Chichewa ndikumalemba ndikuyankhula Yambani Lero, Musadzionele Pasi #fyp #foryou #learnenglish #learnontiktok #malawiantiktok🇲🇼 #tiktokzambia🇿🇲 #viral
iSpeak Learning Platform
Region: MW
Sunday 27 September 2026 10:14:13 GMT
Music
Download
Comments
whyson Daniel :
ndi ndalama zingati
2026-09-27 23:19:20
1
jane :
tipange bwanji ife ndi 0 timasirira anthu akamayankhura zizungu😊
2026-09-28 05:42:41
1
Loveness Namateh :
Ineso ndikuifuna Kaya feels ndi bwanji
2026-09-27 18:11:50
1
Alice saka :
ineyo ndikufuna
2026-09-28 05:40:23
1
Loveness :
ineso nufuna kimaphuzira nawo
2026-09-28 16:44:25
1
maria :
inenso mundipange add ndindalama zingati
2026-09-27 19:15:17
1
Khliyo Akan :
inenso ndikufuna ndizihunzira nawo
2026-09-27 23:02:40
1
Mama blessings :
mkupanga zingati tiphuzireko nawo
2026-09-28 13:56:03
1
Rosechisewu :
ine ndimava bwino bwino and ndimalemba English Kom kuyakhula bwino nkhani ndimakanika
2026-09-27 15:48:46
3
user6026050281212 :
follow
2026-09-28 12:02:29
1
euncekapalamula :
ineso ndikufuna
2026-09-27 18:35:06
1
Evangelist S.Chikopa{It's time :
active
2026-09-28 12:12:15
1
violet thima :
ine ndufuna koma vuto ndi ku user imo Wapdakutheka
2026-09-27 18:58:38
1
nobsmhango :
ine ndilipo
2026-09-27 16:14:20
1
Mariakam :
ndikufuna ndiuzeni zochita
2026-09-28 01:08:05
1
chimwemwe Pvt school :
nice
2026-09-28 03:25:17
1
martha :
ineso ndikuna ndimphuzile nawo English
2026-09-27 16:33:10
1
paul black :
tipangen add tiphuzile
2026-09-28 10:44:13
1
Ferix Sadyora :
Tithandizeni
2026-09-27 18:41:23
1
user33024343791154 :
mundipang jioni lmeneyo
2026-09-27 17:57:26
1
mphatso tayengwa :
fees ndi ndrama zongat?
2026-09-27 17:40:54
2
Eliza furze :
Ti thandizeni chonde
2026-09-28 06:02:58
1
preciousmakwakwa :
tiphuzire nawo zimayenda bwanji
2026-09-27 19:39:11
1
eneles :
ndindalam zingat
2026-09-28 11:09:42
1
Brazio Misasi :
mumapanga zingati
2026-09-28 13:05:20
1
To see more videos from user @ispeaklearningplatform, please go to the Tikwm
homepage.