munthuyu akusowekera mumthu ozindikila bwinobwino kuti azimuyakha inline with his reasons akukambila kut God kulibe.
in answering his reasons do not qoute bible coz waikana, use general knowledge ngt iyeyo.
He is not wrong, angofunikila kumuzindikilisa bas, kumuyakha mafuso onse and then he gets converted. matter settled.
Oooo (Allah) mukhululukileni ameneyu sakudziwa chimwe akulankhula
2026-09-28 07:36:48
0
MWAPHI CHISALE TECH :
zikufunika nzeru
2026-09-28 07:28:08
0
Lucius paul :
otelewa mulungu amawakonda kwambili Moti lero amenei kulapa osamuziwa Ai kulalikira osamukhulupirira ai
2026-09-28 06:24:55
2
borthug mw :
I'm proud to be a Muslim ☪️
2026-09-28 12:48:46
0
Limwaga :
he's critically right
2026-09-28 07:38:48
2
London Clothing Centre :
Pagulu ponsepa akunena chilungamo ndi mdara yu Basitu 🔥
2026-09-28 08:45:39
1
Jay_N :
chilungamo chimenechi
2026-09-28 06:39:54
1
DJ MITHUTHA Mw 🇹🇿🇹🇿🇹🇿 :
DJ MITHUTHA Mw
2026-09-27 20:39:41
1
Malambe :
sitikugwilizana nao but i salute him 4 being real & honest rather than being fake..pretendng as if he blve in God while not...cos ku Malawi kunachuluka ma pretenders