@cathynakoma: kut mukondedwe kwambiri komaso azikupangilani chioichose #MonetizeAccount

cathy Nakoma
cathy Nakoma
Open In TikTok:
Region: ZA
Tuesday 29 September 2026 10:13:33 GMT
86893
2736
122
535

Music

Download

Comments

inno_valinue
Da-min.14 :
ife tikufuna ofusirira , nkaz winawake wandikana kwambir 🥹 plz help kamandiwawa kankaz kameneka😁
2026-10-04 10:10:01
0
patriciakazito
Patricia Kazito :
amuna anga anasiya kundikonda pliz help me azindikonda
2026-10-03 14:42:56
0
user215139815810
Hellen kuleya :
Zikomo inuyo pokhala ndinzelu kuposa allah
2026-10-03 20:18:26
0
charity.phiri92
Charity phiri :
thanks
2026-10-03 03:01:04
0
richardmhonekasar
richardmhonekasar :
Thanks
2026-10-04 03:46:06
0
4th2026
4th Enterprise :
za bodza izi iyaa chikondi chimachokera kwa Mulungu
2026-09-29 16:43:06
11
user3466817088152
Hashim TZ :
🤣🤣koma guys basi kumukaikira mulungu kumeneko mmm
2026-09-29 14:04:30
2
geoffreyphiri141
tardrain delijah :
mayi wina wake akut andiloza ndy ndipange bwnji
2026-10-02 08:30:46
0
user488833166272
Evelyn hannah :
mama kd ungapange anthu awiri pakamoz
2026-09-30 13:43:08
1
labiyah7
Labiyah :
shiriki. zopanga anthu osapephela zaziii
2026-10-01 16:38:25
2
user8592488582250
user8592488582250 :
ndipanga bwana wanga andionjezere ndarama aaalaaah
2026-09-29 10:41:58
0
userfrankm123
Frank Matemba :
Mai ife kuno no mankhwala koma bwana amatikonda kwambiri komanso kuti nthandiza kosa yamba mulungu wamkulu
2026-10-01 17:08:50
1
zaka.m.chirwa
Zaka m chirwa :
ngat after 2 years mtengo wawuma kapena udzu wawuma zikhala bwanji
2026-09-29 14:15:23
1
khimad0
KHIMA :
mmalo.mokondedwa ndipamene umachotsedwa nazo ntchito
2026-10-01 12:20:37
2
bonganmarygondwe
Bongan mary Gondwe :
ndithandizeniko obwezelesa patchito abale
2026-09-29 10:45:55
0
yamiematandaikake
Yamie matandaika Keinie :
kukondedwa ku nchito umakhala kapolo umangotumidwa zilisose ine nde simpanga nawo bola ndupeza salary
2026-10-01 19:02:18
1
kabisaalex493
Kabisa Alex :
ok chabwino
2026-09-30 19:11:11
1
colbyastro
ColbyAstro🌹 :
Zaziiiii
2026-09-30 10:54:48
1
nicechatala
Nice chatala :
zikomo mama tathokoza
2026-09-29 15:08:16
2
zibekekaunga
Zibeke :
iyiyi ndipanga
2026-09-29 13:27:10
1
p.big.guy
P big guy :
Zikomo
2026-09-29 11:43:16
1
robertmwale591
Robert mwale :
ok.
2026-10-01 20:15:23
0
user1065224222165
blessings :
Ife amatikonda kale timakhulupilila mulungu🙏🙏
2026-10-02 02:47:02
0
brenda.tsogolani
Brenda Tsogolani :
musatibhowe zaziiii
2026-10-03 11:12:49
0
user7378184356013
Square :
Okay
2026-10-03 21:21:02
0
To see more videos from user @cathynakoma, please go to the Tikwm homepage.

Other Videos


About