Mukanatha kuwapititsa ku police without kuwaika pa social media, she's even apologizing tatiyeni tizikondana abale, analakwitsa eya koma thaw zina tatiyeni tizikhululuka
2026-09-29 11:45:30
146
Evangelist Cosmas Chizula :
nane zoofoka zanga zambiri 🥹 ndiweluzilenji mzanga😭 akubatu tilipo ambili koma kusagwindwa 🥹 or mukuipatsa motonu zanu kamulu chabe zabisindwa mukuoneka ngati oyera by the way la 40 limakwana kumasamala
2026-09-29 12:02:17
105
Tionah Bou :
mayake a ex wanga awa ex wanga otupa phuno uja
2026-09-29 12:42:50
1
Effie🤎 :
ife ku SDA kwathu taakana
2026-09-29 11:32:55
105
obvious 🤑 :
mukanangokambirana osat mpaka pa social media abale, ndachita manyazi ngat ndmayanga 😭
2026-09-29 11:33:12
76
Glory Babie ❤️ :
Aliyense ndi okuba kungoti inafe la 40 silinatikwanire
2026-09-29 12:12:45
15
Funnie :
nde chovalira dorica ndichan
2026-09-29 11:53:28
1
ZHAYHIE :
km azimai sitimakondana 🙌 eeeeh osangokambilana without involving social media bwnj mmmm pena umunthu uzititsutsa😩
2026-09-29 12:00:56
23
Black-Child 🇲🇼📸 :
wakuba wa mkazi amapasidwa ulemu chonchi?
2026-09-29 12:16:36
11
🧉 :
things can happen unplanned guys , kuba sikwabwino but she doesn't look like someone who used to stole things just discuss outside social media for the sake of karma
tonse ndimbava pano, ena timabera amuna athu, ena kuba kuntchito mwayi sitigwidwa😥😥 izizi zojambulanazi sizabwino
2026-09-29 11:53:30
17
NYADI :
komatu awa si a SDA chovalila nsalu imeney ndichan 🥺
2026-09-29 12:01:08
6
Naomi :
komanso Siwa SDA wangovala
2026-09-29 11:27:13
17
pastorfaith061 :
Koma abale such a beautiful lady 🥺😭😭😭 mwina chiwanda chabe
2026-09-29 12:30:23
5
user6937474685197 :
koma Nomsa eeee ukanasiya kuba please chonde
2026-09-29 12:00:12
8
Augastine ❤❤ :
we learn though mistakes azimayi sibwino choncho inde mayiyo walakwitsa kuba km inuso muli ndizofooka zanu pls abeg iziz tiyeni timphunzile kuvesesana💔
2026-09-29 11:54:02
13
marty :
who knows her please
2026-09-29 11:32:49
5
Canie Candy Cattel :
sakudziwa chomwe achita ndi ang'ono asiyeni🥹
2026-09-29 11:30:36
24
Bongie🖤 :
aba chani abale???
2026-09-29 10:56:30
9
letthemtalk :
dolika ndi ntima osati chitenje
2026-09-29 11:21:38
27
zahira's closet :
aba chani inu ahh nanga simukunena bwanji ah
2026-09-29 11:29:19
8
To see more videos from user @manupage09, please go to the Tikwm
homepage.