@tkhumbanyiwa: #Masiku 381 atatha, malonjezo akumana ndi zenizeni: palibe mafuta, gasi ukusowa, forex ikusowa, mankhwala akusowa, madzi ndi magetsi sizikupezeka mokhazikika, ndipo anthu aku Malawi akugona kuma station a mafuta kuti apeze malita ochepa. Tinauzidwa kuti pali njira zothetsera mavutowa; tsopano anthu aku Malawi akufuna mayankho🇲🇼 381 days later, the promises have met reality: no fuel, gas shortages, scarce forex, medicine shortages, unreliable water and electricity, and Malawians sleeping at fuel pumps just to get a few litres. We were promised solutions; now Malawians need answers🇲🇼
Nthanda khumbanyiwa official
Region: MW
Friday 02 October 2026 19:34:30 GMT
Music
Download
Comments
jestinaholea :
ndalama mmene zikusowela heeee.
2026-10-02 20:52:46
6
R C mayaka Mvula :
Politicians have fooled us, I have learnt a lesson
2026-10-03 01:56:48
1
Amuna Maloya :
sisitu likutha ngati mamuna
2026-10-02 22:39:21
1
virg :
inuyo ingopangani zoti mafutawo abwere mesa inu ndochuluka nzeru
2026-10-02 20:49:39
25
Mwai Noah :
I was there lero koma the queue was too much. This is good reporting, chomvetsa chisoni ndichoti sakubwela kuzatiuza kuti mavutowa akuchitika chifukwa chani. komanso Iwo omwewa anati akakweza mitengo yamafuta sadzasowanso koma si izi? Mera olo kumapanga post fuel schedule ayi ndithu
2026-10-02 23:04:12
1
mercy :
Malawi kuvetsa chisoni
2026-10-02 21:01:28
1
Dr George :
Ndiye solution nkutani ,??
Nenani
2026-10-02 20:49:17
7
Gerrard chilumphagerrard@gmail :
Ati tizithilamo sima mmangalimoto
2026-10-02 20:23:22
5
Tricia -tricia💜 :
kom nde u look like tuno hun🥰🥰
2026-10-02 19:47:28
9
FED :
uyuyu ndimangomukonda popanda chifukwa ,,,, top fan wako ine
2026-10-02 20:56:06
3
Favour Magereta 🇲🇼🇲🇼 :
kumaliopa mawa straight 💪💪💪💪
2026-10-03 01:37:56
2
Blaqe :
Ine si wa Dpp koma chilungamo chiyende ngat madzi mafuta akusowa padzilo lonse lapansi chifukwa cha nkhondo yaku Iran. Pali ma nkhani ngat a magesi, miseu etc tikambe zimenezo. otherwise nkhani ya mafutayi musanamize amalawi kuti Vuto ndi Dpp.
2026-10-02 21:53:28
4
Luka Paul :
mukunamatu inu ndili ku nampula panopa ndimakumba mijigo koma panopa ndikutha mwezi mma filling mukungokhala mopanda mafuta sikumalawi kokhako ayi ndipo mundikhulupirire nkhani yamafuta ndi paliponse
2026-10-02 21:03:02
3
Kantala :
Bola izindizuza DPP osati MCP
2026-10-02 22:32:36
1
Drew :
masiku 381 days 🤣🤣🤣
2026-10-02 20:25:49
3
Tamah♥️ :
Eya timafunika tidzikumbutsanadi amalawi timayiwala😅😅😅😅
2026-10-02 21:23:00
2
kelvinator :
komaso iweso unaimila DPP yomweyo zinavuta kod wagalukila
2026-10-02 21:48:35
0
Maya Kachala :
Ndipo nde ineso N’nakapanga park pa Puma yanjira zaku immigration. Watched the tanker kutsitsa mafuta nkunyamuka- nkumati sitingathile ndiopanga kale book ndianthu aboma🙌🏾😂😂 eh!
2026-10-02 21:14:01
0
eliudkatandalira :
yes but now is better. we can stand on a cue for a short time as compared to that time the whole week
2026-10-02 20:59:03
5
SCII :
Direct attack! love the reporting Ntha🔥
2026-10-02 20:31:09
5
copper :
machine
2026-10-02 20:33:53
2
seen.2_ :
“Mawa kumaliopa”…. Those words will live rent free in many Malawians minds
2026-10-02 21:06:17
2
2k :
Kukakamira town kuno akupezeka palipose
Vuto town ma galimlto azazamu enawo atumizeni ku mudzi sasowa mafuta
2026-10-02 20:48:19
0
Maureen Kalinda :
akaoneke anzeru lero ndi izizi tonse tuvutika😂😂😂😂under proven leadership 😂😂
2026-10-02 21:13:47
1
alinafechapola576 :
active😃😃😃
2026-10-02 20:56:46
1
To see more videos from user @tkhumbanyiwa, please go to the Tikwm
homepage.