@fannyshaba906:

Memox
Memox
Open In TikTok:
Region: ZA
Saturday 03 October 2026 10:57:02 GMT
77405
3057
1398
188

Music

Download

Comments

user6193580390425
Cathy Hamela :
kd simungakambeko nkhani yoti athu atembenuke mtima mwakulatu izi sizikukukhalani mayi
2026-10-10 09:55:48
3
bravengalawango
Brave Ngalawango :
yankhulani Za zeru Mayi ndinu akulu
2026-10-09 12:23:15
1
phirigrace87
Phirigrace :
zopusa basi
2026-10-09 11:31:14
0
fundo2592
Fundo :
Ngati uli wa ulemu bwanji uli single?
2026-10-10 03:33:38
0
chrissygrant75
Chrissy Grant :
odi ndikupange follow mamie 🤣🤣🤣
2026-10-09 17:59:20
1
lozigwanza
Lozi Gwanza :
ndipotu akatero amabwererabe Kwa ine after kukuvulani kkkk
2026-10-03 18:54:02
34
salobeib
Salome Thozzer :
kuona akuyankhulawo nkhope itaserereka ndimankhwala aboma
2026-10-05 11:23:02
26
walucrochets
LUH SHAWTY 💎✨ :
how to make money???
2026-10-10 13:23:22
1
marium.chanza
marium chanza :
mai ndinu opusa kwambiri
2026-10-04 11:56:47
25
atumary11
atutu :
ineyo sindinakhaleko pabanja koma sindinga nyengane ndimamuna okwatila
2026-10-06 10:45:09
12
bitia02
Bitia :
Za ziiiii
2026-10-04 05:37:32
42
user5538273872354
wapona :
koma nkhope za ma mg2 🙌🙌🙌
2026-10-04 08:35:26
12
maggiephiri603
Maggie Phiri :
Koma abale asiyeni mankhwala amwa kwambili
2026-10-05 18:57:37
7
user3397037146794
Steven Phiri :
mg2 mzanga oyeeee 🥰🥰
2026-10-03 19:26:58
10
grace.gift.m
grace gift moyenda :
mg2 woyeee pano mwana wachaka
2026-10-04 10:29:29
9
theunshakablequeen
MandaZelpha🩷 :
ma MG1 anzanga muli pati
2026-10-04 10:25:32
13
emery8136
Emery 👗 :
uhuru basi amunanu anapita kuti kodi
2026-10-04 14:02:22
6
gracebottoman346
Grace Bottoman :
ndiye tonse tingokhala ma mg2 bwa tione kuti zizitha bwanji chifukwa mg1 sikuti iyeyo u mg2 sangakwanisetu ayi chifukwa zkuoneka kuti u mg2 ndiwa ulemu mg1 mwano tonse tingokhala mg2 tonse tikhale aulemu apa iya
2026-10-04 14:34:43
7
flowless815
flowless👅 :
Za ziiii
2026-10-04 06:47:25
12
gracewalanijere
Grace Walani jere🥰🥰🥰 :
Amuna angokusekani kut mukuona ngt ndingasiye mkaz wanga kukwatira inu[Laugh approved]
2026-10-03 23:42:29
10
anaphiri08
AISHAH BINT LEONARD :
kkkkk abale popangira VN ndipati ,,koma mukudziwa kuti akakuvulani mkukuonani uchitsiru wanu amabweleranso komweko ku MG1 ,ndiye pamenepo chitsiru ndi ndani?amakufunsirani inde sikophwesera mtima ngati watupa ndi heartbreak.
2026-10-04 12:31:24
13
lizzy6598
Lizzy :
Malangizo osamangilila mulungu akakulangani nazo izi kuchemelela zosakhala bwino😭
2026-10-04 13:54:32
6
hannahluka02
Hannah Luka :
ndimaona ngatitu mukufuna mufotokoze za nzeru km ayi usandiyakhulise pambali km uzikoze wekha ine amene akufuna kulanga mg2 andipeze ine nsimasekelela amunawa tachoka nao patali 🥰🥰🥰🥰🥰
2026-10-05 07:12:29
11
user4011866777341
halunimdara :
ndichifukwa chani mg2 amawasiyaso kubwerera kwa MG 1
2026-10-04 11:19:14
5
To see more videos from user @fannyshaba906, please go to the Tikwm homepage.

Other Videos


About