Language
English
عربي
Tiếng Việt
русский
français
español
日本語
한글
Deutsch
हिन्दी
简体中文
繁體中文
API
Home
How To Use
Language
English
عربي
Tiếng Việt
русский
français
español
日本語
한글
Deutsch
हिन्दी
简体中文
繁體中文
Home
Detail
@apostlemilliondaniel: #onthisday
apostle Million Daniel (CRC)
Open In TikTok:
Region: MW
Saturday 03 October 2026 19:28:28 GMT
35424
759
138
136
Music
Download
No Watermark .mp4 (
16.53MB
)
No Watermark(HD) .mp4 (
16.53MB
)
Watermark .mp4 (
28.6MB
)
Music .mp3
Comments
mauee6 :
tili busy ndikusaka ndalama Ku Malawi kwavuta uphawi,ma feeling ndi njala😂😂😂😂
2026-10-04 17:30:33
4
tapiwa :
Ine pano ndinaleka kalekake
2026-10-04 10:41:01
0
jane msukwa :
ndizoonadi abusa ine pano ndinazolowera pano chilakolako chinatha kale kale
2026-10-04 18:16:50
2
edithfraction :
Amen mwaona ine
2026-10-04 13:48:15
1
Hassina Jayson :
ngati mwaona ine
2026-10-04 11:26:43
1
charity Kapachika :
kumwamba kwayakhula
2026-10-04 12:21:05
3
Dada kay :
kuno tukhala ngat brother n sister tikangodya basi aliyese kuona pokagona 😭😭panopa ndazolowera koma ppoyamba ndimakhala ndimafuso koma panopa mtima wanga unalimbaso
2026-10-03 23:32:25
5
Mirriammbale :
Mulungu atichitire chifundo ine ndi amunanga chifukwa cha long distance koma timakondana (financial yikutipatulitsa🙏)
2026-10-04 12:13:25
5
Beatrice lingoni :
Ambuye pitilizani kutipangisa kukondana mpaka kare🙏🙏🙏
2026-10-04 16:50:09
3
kaitagyyum5 :
ndili ndi friend wachizimai, akuti mwamunake amatentha thupi akatuluka kunja,mnyumbamo aliyense chipinda chake, moti 3 years samagonana.
2026-10-04 09:40:11
0
user871906119037 :
Abusa ine zaka 6 ndi miyezi abusa kenaka ndi chimwa
2026-10-04 12:14:42
3
kafileni :
muku yakhula ndi ine ndendende apa tikungogona mutima ukuwawa kuti uzimuwona amene akugonana naye chilakolako ndilibe
2026-10-04 06:58:11
3
mama favour🥰🥰 :
mwayakhula ndi moyo wanga abusa mulungu afikire nyengo zanga lero ,
2026-10-04 03:03:34
3
LoveLo🌹😍 :
ambuye atichitile chifundo poti Santana wamanga thenje timasuleni ambuye🙏🙏
2026-10-04 06:01:04
2
Dave Chirwa :
Yanga inatha timkakhala nthawi yaitali mwina one week or 2 weeks ine ndinali nd mkazi wina kunja
2026-10-04 04:36:33
2
VELLNTN BILLYT :
ameni 🙏🙏🙏
2026-10-04 02:01:06
1
CHIFUNDO CHINA :
chiyambireni sinakumane mwachindunji ngati iyi 💔
2026-10-03 22:28:03
2
switcalli :
amen
2026-10-04 05:49:49
1
mercy mj kang'oma phiri :
Mulungu andipatse chisomo, tili limodzi, koma palibe chimachitika, timangoyang,anana basi, Ambuye andiyendele mwapadela dela
2026-10-04 15:19:06
1
Lommie Tembo😇😍 :
amen
2026-10-03 20:39:00
1
Mrs Nathan Munthali :
A Busa uthenga uwu ndi waine 😭😭ndi kukumanaso nazo ine
2026-10-04 06:54:15
1
Peace💃 :
Amen abusa ndipempherereni please
2026-10-03 20:36:50
1
Mayra beibs😘 :
Amen abusa mukulankhula ndineyo pano😭😭🙌
2026-10-04 01:10:32
1
suzen oswad :
ineso mundipemphelele please🙏
2026-10-03 20:23:48
1
user5984140717771 :
ambuye atichitile chifundo khondo imeneyo jaikulu zedi ,mumabanjamu makamaka ife azimayi. chifukwa azibambo akuchulusa zibwezi ndeno tilkamava zimenezo chikumbutima chimafa .mwalakhula ndimoyo Wanga ndimakhala Olo 6 madzi ndili pogona popo , ndimakhala chifukwa chilakolako changa chinatha Pano nikunena Pano tilipo awili moti ine napanga chisakho chothesa banjalo basi.abusa tithanfiseni moyo Wanga waudzimu
2026-10-04 02:56:04
2
To see more videos from user @apostlemilliondaniel, please go to the Tikwm homepage.
Other Videos
Loki Season 2 First Poster!! #loki #mcu #marvel #movies #fyp
Nana patekar laughing Memes Templets video 🤣 Fanny laughing
balançar pra não pegar dengue né 😂 #agua #carnaval #fatalmodel #fatalmodelcortes #fatalmodelcy
Muốn chăm sóc mi, mày, tóc mà tiết kiệm hơn? Tham khảo ngay phiên bản này nha chị em #serumusma #duongmimay #chamsocmi #chamsocmay #chamsoctoc
Name nala la #namenamala#diggdole #massambawalo #amadeus
About
Robot
API
Legal
Privacy Policy