@ishmaellosani: Phunziro: Nyani ndi Kamba adatola mbewu ya Nthochi mumtsinje. Adagawana, Nyani adatenga mbali yakumtunda (kwamasamba obiriwira) pamene Kamba adatenga mbali yakutsinde (komwe kudali mizu ndi madothi). Onerani kuti mudziwe chomwe chidachitika pambuyo pake. Pangani follow Ishmael Losani "The Explorer" kuti zambiri zisakuphonyeni. #MeetIshmael #Phunziro #Nyani #Kamba #Nthochi
Ishmael Losani
Region: MW
Wednesday 07 October 2026 22:15:41 GMT
Music
Download
Comments
charity sibawo :
amen 🙏 mulungu atitsegule maso ndi zelu za uzimu kt tizidxiw
2026-10-08 03:32:39
5
king k winner :
his true
2026-10-08 00:11:08
2
Fredrick cross :
this is interesting
2026-10-08 04:05:51
1
zione bwande :
phunziro la Bwino mulungu akudaritseni 🙏🙏
2026-10-08 04:52:48
2
Faith 💜 :
phumzilo lapamwamba🙏
2026-10-08 05:48:29
4
marynkhoma925 :
amen tizikhala ndimtima wachikondi
2026-10-08 02:17:24
1
chritonmkwetemba :
Apandamphuzilapo kathu
2026-10-08 03:59:15
4
saidi :
kma zona
2026-10-08 02:39:08
5
fatima :
zoona izi
2026-10-08 03:08:59
2
Esteva Nepiyara :
ndizoona
2026-10-08 03:02:46
2
CHEMBE cha jodzi :
nice
2026-10-08 02:31:46
3
Takondwa Flackson :
His true
2026-10-08 04:14:31
1
Gloria beib :
amen
2026-10-08 00:49:40
2
Jacqueline kalisilila😍🥰♥️💞 :
ndipo zoona
2026-10-07 23:36:42
2
Junior Julia's mhone :
exactly
2026-10-08 04:07:19
1
Mercy Leonard :
ameen
2026-10-08 00:26:40
2
p end p :
zikomo taphuzila
2026-10-07 22:21:27
2
Catherine Phiri :
amen
2026-10-07 23:07:29
2
Phatso🥰 :
mulungu mundisogoreli amen 🙏🙏
2026-10-08 05:52:21
1
kenam douglas :
ndizimenedi zimachitika
2026-10-08 02:57:02
1
Alfred Josayah :
Ambili ndinagwa mumavuto chifukwa chofela maonekedwe zikomo chifukwa cha malangizo awa 🙏
2026-10-08 07:27:41
1
fulolida lanjensi :
Zoonadi zimenezo brother zikuchitika zimenezo chifukwa chosafuna wina achite bwino
2026-10-08 06:42:12
1
user15796315625037user15796315 :
100/100
2026-10-08 10:18:31
0
OBERT phiri83 :
amen amen
2026-10-08 10:34:45
0
ma pee :
ZOONA mphuzizitsi
2026-10-08 03:16:10
0
To see more videos from user @ishmaellosani, please go to the Tikwm
homepage.