Ndimakumbuka Hon Suleiman ndi ena a dpp nthawi ya campaign....ankat zankhondo zakunja sizigwilizana Ndikusowan kwamafuta ndipo a Chakwera akubisila dala mafuta ...iwo akatenga boma... adzathana nazo within 6 months....
Nde pano aliduuu osapezekanso pa ground kut apange update anthu ngat dziko.....
Andale 🙌