khani iy ndiyoona 😭😭😭😭😭😭 amuna aku jon parbe amene ari single
2026-11-10 21:25:12
0
Nancy mkandawire🥰 :
zikungo fanana ifeso tikuyengedwa asisi
2026-10-09 20:33:20
22
Mike Edward Sitima :
😂😂 wangoyankhula chilungamo basi
2026-11-09 12:55:04
0
Esther ♥️ Gersson🇲🇼 🇿🇦 :
Aaaaaa mbili ya kale imeneyo asisi pano azimaiwoso ku Malawi ko akunyengedwa ndinthu pano ndi 50 50 🤣🤣🤣🤣🤣🙌
2026-10-10 10:58:58
13
Benson Banda :
ndekuti iweso uligulu lochindidwa chifukwa nzimayi wabwino bwino sungamayankhule chichewa ngati chimenecho pamwa pako za uhure basi
2026-10-10 05:44:26
28
BOCCO MW :
azimai nanu mukunyengedwa zooti muli nd azimunanu komwekuno simusamala at munabwelera kusaka nde amasaka nd kunyelo? [Heartwarming][Heartwarming]
2026-10-09 19:22:06
5
jennifer malenga :
nanga angalime ntchito ndiyonweyo[Tears of joy][Tears of joy][Pray]
2026-10-09 18:58:03
5
surprise :
ndipo ndiye tinyenga zenizeni
2026-10-09 20:01:15
1
Alex dzonzi :
Moti iwe akunyenga😅
2026-10-09 15:10:36
11
planBmalawi :
Nde ndikukwatra iweyotu Mesa wathetsa banja langa😭
2026-10-10 14:54:12
1
Brian masacheh :
sopano mchira ntchito yake ndichani?
2026-10-09 19:36:56
1
kettie :
Ine mamuna sangandisiye ku Malawi lithepo bwa asaa
2026-10-09 16:09:05
1
promisebeby :
ifenso tizichindisa iyaa[Tears of joy][Tears of joy][Tears of joy]
2026-10-10 18:38:44
1
Chimwemwe Mapwesera :
Ndipo nde sukunama onse akudikilira theba ndiopilira koma azibambo nde ntchito akuigwila
2026-10-10 08:30:52
0
Khadidya Linje :
zoona
2026-10-09 20:56:50
1
mikhe chipira Adera :
Udziti Azimunanu kuno nde Akutichinda 🤣🤣🤣😂😂🤗👋
2026-10-11 07:00:07
1
tasmim beib ❤️❤️ :
kkkk
2026-10-10 14:03:44
0
GODFREY NJOVU YALEMA 🇲🇼 :
akutuma
2026-10-09 16:32:51
2
Islam idanna Fahad :
kkkkkkkk nanga ndingalime bebi ndiyomweyi
2026-10-09 19:56:31
3
Lopi son's 1 :
nde zinthandiza chan ngt dziko
2026-10-09 21:25:04
1
aishah M 😍😍 :
Ndipo live. Ndinakhalapo 4 years kudikila Jon no chibwez. Koma atangondiyitana kupita ku Jon mmmm 😭kuzandikwatilila mzula koma ine ndinali pamavuto mix sindimagwilas tchito mm. Pano kudikila so theba🙌
2026-10-09 16:45:30
2
Joso G Chimphwanya :
live[Big LOL]
2026-10-09 14:37:59
1
peter mike :
eya ndifuna ndizinyengana ndi iweyo
2026-10-09 20:44:27
1
AREA 51 ⚠️ :
then what you want therm to do though
2026-10-09 13:18:09
2
To see more videos from user @win.mathews888, please go to the Tikwm
homepage.