@sirgodfreyonlineclasess: Replying to @004wongiee 🦷😂 DENTAL CLINIC KUMATAA! OSACHOTSETSA AYE! 🤣🔥 Mano anu akufuna chisamaliro? 🦷😁 Musadikire mpaka vuto litakula! 😂🔥 KUMATAA OSACHOTSETSA! 😁 Smile with confidence! 🦷✨ #DentalClinic #Dentistry #SirGodfreyMalata #MalawiTikTok #FYP 📞 0882 709 843 / 0882 374 025

Sir Godfrey Online classes🔥
Sir Godfrey Online classes🔥
Open In TikTok:
Region: MW
Sunday 11 October 2026 13:45:16 GMT
140387
4156
528
265

Music

Download

Comments

lamzy.magombo8
Lamzy Magombo :
Amene muli ndi dental clinic around Area 25 or 49 kumata dzino lobooka ndizingati??
2026-10-14 12:39:58
2
lovehsamson
Loveh❤️ :
ineyo dzino linafuna kundipha amwene kwa tsiku limodzi lokha koma ululu kuposa ku Labour
2026-10-13 14:10:12
3
user58762050094780
brigadier . Jojo :
ine limodzi ndidachosesa koma linanso labooka, ndiye ine pano ndili ku machinga nditani kuti thandizo lanu ndilifikire clinic yanu ili kuti?
2026-10-13 00:10:46
2
mrs.maliro
Mrs maliro :
Ululu wa dzino palibe angandiputsitse kuti nsachotsetse kuli bwino nkhale ndi magweru ndili ndi mtendere
2026-10-12 07:49:24
41
funnyephraim955
Funny Ephraim :
inu ine mmafuna kunyeledwa kuli kuwawa kwadzino apa nduchokela kochotsa ndipo ndachotsa awiri pano mtendele okhaokha
2026-10-13 08:52:44
2
abgailevance
Abgail namasina Evance :
Ine ndachotsako atatu apa Lina layambanso lipitilila sindichitira mwina koma kukachotsa
2026-10-13 08:02:22
1
user9755584873483
PHIZEY CATERING :
inuyo sir mwalankhula bwino koma mvuto ndi matchajidwe andarama mmene mumang,ambila mtengo nde ambirife timafuna kwambiri koma timalephela kufikila
2026-10-13 03:40:20
1
wamaca7
wama🥰ca :
simunadwaleko dzino zikomo kumpando🧎
2026-10-11 15:56:27
13
loveness.mwazera
Loveness Mwazera :
ine kuno ndachosa 6kumata zimapezeka lawawaso bola kuchosa bro
2026-10-11 15:59:57
9
vishu8723
vishu :
Dzino limafika Poti ulibe option than kuchotsa zonse munenazo need money a lot of money palibe treatment yodhula kuchithu chaching'ono ngati dzino ine pano onse anathamo
2026-10-12 07:10:29
6
maxwelljossam
Maxwell Jossam :
Mukuyankhula chifukwa Chiwowa mtima wa chikondi pa munthu zanu dzino kulimata lilibe 5years lisanayambe kukuvutitsa ndipo chomwe mukuyang'ana inu ma doctors a dental ndi ndalama osati kumuchotsa nzanu uluru Palibe option ina kuposa kuchotsa dzino kuti muthane ndi uluru omwe imagwira ingakhare khosi lanu kukanika kutembenuka ndipo zikapitilira zimaoanga affecte ubongo wathu chifukwa ndi mitsempha yomwe imatiza uthenga oti kuli ululu zomwe zimatha kulamura mtima kuti usiye kugwira ntchito pamenepo munthu amakhala wakomoka ndi uluru penaso amatha kupitilira imfa ndi yomweyo Kachotseni dzino amene amadziwa kuipa kokhara munthu okunva ululu usana ndi usiku
2026-10-12 07:55:37
10
user3286381847823
Grace of God 🇿🇲🇲🇼 :
ine yanga imangopweteka koma ndi losaboka losagwedera lingowawa 😭😭😭😭😭😭 kukanika kugona Inu ine
2026-10-12 10:54:16
5
mariamfarook271
Mariam Farook :
ine ndinachosa kale 4 kaya atha koma ululu wazino mmmmmm
2026-10-12 04:53:31
9
princessnthanda1205
Princess Nthanda❤️ :
adokotala ,sir malata
2026-10-12 06:51:10
1
memory0318
Memory :
Ine ndimafuna kutsuka ndi bwanji?
2026-10-12 08:29:42
1
cosmasmagwazeni
cosmasmagwazeni🇲🇼 :
mungalalikiletu bwana, eeee
2026-10-11 16:40:22
1
watisonphiri270
Wandi phiri :
next
2026-10-11 16:19:15
0
manual.njemusi
Manual Njemusi :
Ine Mano mpaka 5 koma Rina rikupweteka eshii
2026-10-11 19:44:08
0
samuel.bonongwe0
Sam praise :
kd kumata zino ndindalama zingat boss tiyakhulen tithandizeni
2026-10-12 07:54:57
3
bridgetziba8
[email protected] :
nanga mulikuti?
2026-10-11 20:14:12
0
stevenkandiero
STEVEN :
Muli kuti clinic yanu
2026-10-11 16:11:48
0
andilea.demis
Andilea Demis :
inu mukupezeka kut
2026-10-12 08:38:37
2
user6861285420425
Gina💕💕💖💖 :
lulu wa dzino ndilibe nalo mawu ndipo ndikuona akuthamo
2026-10-12 09:02:30
3
chrissie.kapherach
chrissie kapherachoka :
simunadwareko dzino inu
2026-10-11 21:01:11
4
faithmasanza721
Faith Masanza :
ine anga amachokamo okha tu
2026-10-11 16:40:30
0
To see more videos from user @sirgodfreyonlineclasess, please go to the Tikwm homepage.

Other Videos


About