@williamsmasaukoboyisi: scorchers ikagonjetse Zimbabwe pa kwawa adzadelera ana aja. pa 13 pano ku Harare .akuzimbabwe sadzayiwinaso malawi ndanenandanena. remember on 9 October 26 malawi defeated Zimbabwe 🇿🇼 . Malawi 🇲🇼 2 vs Zimbabwe 🇿🇼 0 . apano amalwi akupita ku zim kukawavavadira pa kwawo.