bwanji masiku ano sindikumalandira ma notifications anu
2026-10-26 17:50:48
0
user7019200450104 :
Sheikh zonse mwalakhulazi ineyo zikundichitikila mamuna wanga kumuona nyasa ngati ndithese banja koma iyeyo amandikonda koopya koma vuto ndineyo 😭😭😭😭 ana anga amakonda kwambili koma ndilibe naye mwana kungonva mau ake ine kunyasidwa
2026-10-13 18:15:15
1
phatima :
same here mmmmm zikundidabwisa walah
2026-10-13 15:14:21
0
Kia beib Mrs me😘😘😘😘 :
Mashallah Sheikh chimodz modz mbali yakuno eeish sizikuyenda