@robeib: Replying to @user4490291611554 #southafricatiktok🇿🇦 #zambiantiktok🇿🇲 #malawiantiktok🇲🇼 #akatundu#

Robeib
Robeib
Open In TikTok:
Region: MW
Saturday 17 October 2026 09:59:54 GMT
21806
486
67
90

Music

Download

Comments

nichollasangella
Nichollas Angella :
dzina lina ndichani??
2026-10-17 12:28:14
1
usernancy930
@Nañcy-Mpuwe :
ndili nawo ntengo kwathu madabwa mayanga anandiikira bag kut nziyenda nako😂 mundigure ku Lilongwe
2026-10-17 15:01:00
1
doricamangwazu923
Dorica :
zikomo sister
2026-10-17 17:03:56
0
angamaso2
Patricia nsopela :
koma ungaupeze kuti
2026-10-17 12:50:50
1
user198165868762
mai anu owapeza :
ndipo zoonad ineso n mboni usiku ndikagona ndmava kukoma zot chiyambileni sinamvepo, kma pano nditamva za mpoloni kumasamba wina ndmaika pansi pa pillow pano zinasia sizimachitika ai, zikomo kwambiri mama
2026-10-17 17:08:57
0
tawienahuwo
BabySunShine❣️🖤 :
palibe amene Ali ndi photo ya mtengowo...ine sindikuwudziwatu
2026-10-17 17:09:31
0
myasuwema
tinatumanje11 :
in English mpoloni ndi chani
2026-10-17 12:21:21
1
franklindenson
franklindenson :
Amai ndamva ndipo ndichita ndipo Amai. Kodi ukhoza kuika pamene ukuika ndalama
2026-10-17 14:20:34
1
doreenchatha1
doreenchatha431 :
zikomo
2026-10-17 15:13:54
1
user129431007143
Bertha chabotbertha :
ineyo ndkulila nayogenipano anzanga amakaoda tsindistiku komaine mmmmmh.sizikuyenda or ndtaoda zokongola 😭😭😭😭
2026-10-17 12:47:21
1
hawamu1
chalamandahawa :
ndipo zoondi fiti siyelekez
2026-10-17 11:42:32
1
robeib
Robeib :
ameli uli nawo minda kaya pakhomo ukhoza kuyamba business kugulitsa 😅😅
2026-10-17 10:01:19
2
johnkamwendo330
Mimi :
next
2026-10-17 16:32:05
0
martharpondiya
Marthar Pondiya :
ndichani kodi
2026-10-17 10:30:10
1
jinnynamanja
Jinny Namanja :
Ndathokoza zkm kwambili ndiusaka zitheka business yanga amangondikawa
2026-10-17 12:14:52
1
marthaallinah
Alinah :
Zikomo
2026-10-17 12:47:41
1
franklindenson
franklindenson :
longosolani time bwinobwino
2026-10-17 14:15:43
0
user9081399726324
Joseph machine :
Tatumizani mtengo wake wampoloni anthu awudziwe chifukwa ena dxinalo likuwazunguza chifukwa madera osiyanasiyana amatchula dzina lina
2026-10-17 14:08:39
1
lsaidahmw
Lsaidah :
kod masamba ake uthaxo kugwilisila tchito kusambaxo
2026-10-17 14:39:32
1
user901222135957
Lucy M banda :
mpolon mteng wake umaoneka bwanji
2026-10-17 12:26:38
1
mariam.bulla
Mariam bulla :
olo pamene timaphikila zigege poti palibe poika kaya kuika pamoto
2026-10-17 10:30:15
1
franklindenson
franklindenson :
Kodi ukhale wowuma okha kapena ngakhale wawuwisi
2026-10-17 14:23:20
1
whitebanda5
White :
Tiri ana timapangira mfuti mtengo umenewu 😂😂😂
2026-10-17 13:58:14
1
user9081399726324
Joseph machine :
koma muchichewa ndi mpoloni
2026-10-17 14:09:36
0
ethel.mussah
ETHEL MUSSAH :
umafunika mtengo ouma okhaokha??
2026-10-17 12:43:40
2
To see more videos from user @robeib, please go to the Tikwm homepage.

Other Videos


About