ndiye fuel azayenda bwanji Dec eeeee ,zinthu zake tizithawadi dziko lililatu ,they are forgetting kut ndikuchiduswa kwa fuel
2026-10-21 19:48:36
0
Rhyra❤️ :
iiish kukanika kupita ku mudzi because of seu iiiish 😂
2026-10-22 12:30:57
0
vee💜🤍 :
basi apa sidzapitaso kumudzi kwathu ku Karonga yooh 🙌
2026-10-22 15:46:48
0
nyantalula :
ambuye mu dzitetezera ma driver onse mudzina la yesu.🙏
2026-10-21 18:33:35
3
Sponyonyo :
pamene wafika chiweta atha kupangilamo movie ya Wrong turn
2026-10-18 20:16:37
175
Kim Nanah :
koma kumudzi kwanthu ku rumphi ndi karonga tizapitanso 😭
2026-10-22 10:51:39
0
wezi thindwa :
zoti it used to be a good tarmac road ngati bodza
2026-10-21 18:28:30
1
Miss Kamfo🤎🌸 :
Koma ndizapitaso kwathu Ku lilongwe ine? 😭💔
2026-10-20 04:01:22
1
Apostle Peter Michael🇲🇼🇲🇼 :
What about when the rain comes! eish
2026-10-18 18:07:01
36
Raddie16 :
Just start worshiping the Lord ukalowa mu chiweta
2026-10-18 22:11:33
30
👑Mrs_Mpango :
Ukuku was supposed to be the first section of the road they should have fixed because yhoo ha ah
2026-10-19 04:01:12
47
Evie😘 :
And then I have to be in Karonga next year January amwene mmmm
2026-10-18 21:43:36
13
Ronald. :
this road ukhoza kugona limodzi ndi anyani sure.😂
2026-10-18 18:38:59
9
WILLS DESIGNS :
Iyiyi nde ndi Death Trap like for real yoh...
2026-10-18 21:58:21
3
Ray-G :
ine sindinaone dziko lolephera kupanga manage zinthu ngati malawi. zibwana zeni zeni izi bolanso ministry of transport yo kungoichosapo basi ilibe phindu
2026-10-19 17:11:30
13
Lonjezano :
where's the road koma kunoaaaah
2026-10-18 21:19:45
6
Niephar.🦋🤍 :
Eeh nsewu wake umene nde zima truck zimenezo yoh💔
2026-10-18 18:36:11
6
❤️MakeAya’s Collection 🛍️ ❤️ :
🙌🏽🙌🏽🙌🏽🙌🏽this place haha sindizamuyiwala Muchiweta ine Eeeeeeehh
2026-10-18 18:08:27
2
Mkango_🦁🇲🇼 :
Tikusekerela zopusa we need to act our government has to do something
2026-10-20 07:14:34
0
priolenge_ :
this is the exact place the car tyre decided to do stupid things💔 and it was only me,my mom and cousin💔💔
2026-10-19 13:01:14
4
Destiny brie :
but minister of transportation and road traffic akuyenela kupanga chinachake abale not every year tizikamba iziz zoona ,koditu Pali zithu Zina anthu amaiko Ena amakanika kukuthandizan because ulise kupanga chiganizo mwasanga ngati izizi ayi ndithu soon kukhala mvula
2026-10-19 08:46:33
2
boynazmsukwa :
and the rainy season is coming 😂😂😂, this road will be closed
2026-10-20 12:20:47
1
glory 💋💋 :
As someone who comes from karonga and goes to school Ku Zomba nthawi zonse ndimakhala ndinkhawa Pena sindufuna nkomwe kupita Ku nyumba. ndipo ine I said kuti ma highway anaikidwa mu Lilongwe muja could have waited Kaye akanayamba nseu uwu coz this road is a death trap. mmene magalimoto amatelerera nthawi ya mvula mmenemo mmmhu Mulungu yekha
2026-10-19 21:54:10
1
🦋Lili🦋🌺 :
ndipo this road eishhhh
2026-10-18 19:51:18
2
NYASULU 🐊🫥 :
at death trap
2026-10-19 08:59:53
1
To see more videos from user @_refy, please go to the Tikwm
homepage.