🔥🔥🔥🔥🔥 You are getting somewhere brother. A true leader in the making.
2026-10-19 19:46:17
1
mervisblcumpolota :
jomo ndi machine 😂🤣
2026-10-19 08:41:34
1
yoh :
Respect bwana mayor
2026-10-19 12:30:01
1
Jane mapazi :
Malawi ingatukuke anthu atayamba kuganiza ngati Jomo.,....inetu siine wwa dpp koma Jomo, eish, uyu ndi dolo
2026-10-20 12:10:03
1
Dennis Makumba :
Inetu poyamba Jomo sindinkamumvetsa, KOMA PANO I PERSONALLY UNDERSTAND THIS GUY, ANTHU NGATI AWA NDI AMENE TIKUWAFUNA MDZIKO MUNO, OSATI OPHUNZIRA KOMA OPANDA NZERU.
2026-10-20 09:11:10
1
KABOTA D.F.ZU :
A JOMO NDIMAKUNYADIRANI HEAVY, NDIKUMBUKEKO KOMA TIMAYENDETSA MINI BUS NTHAWI IMENE IJA TIKUPACHILIRA PA MZIKITI PAJA. (AMBUYE AKUDALITSENI ) NDINE ZUZE BWANA JOMO
2026-10-19 07:42:47
1
zahir chitambi :
mawu
2026-10-19 00:23:15
1
To see more videos from user @lhomwe_television, please go to the Tikwm
homepage.