izizi ndinakumananazo , ndikanyamuka ku Blantyre kukafika ku liwonde. amkati nditumize ndalama ndimawakomedwetsa mpaka ndinafika pa police ya liwonde. nkhani yake ndende mmene ikufotokozeledwa. kufika ku police kufusa , anatiyankha kuti za nkhani imeneyo sitikuyidziwa. tinangodziwiratu kuti mbava. chomwe ndinadandawura ndi fuel amene ndinaononga.
2026-10-20 05:18:53
0
user651683663561 :
mzanga iwe😅😅😅
2026-10-20 04:53:40
0
mildah49😘 :
😂😂
2026-10-20 05:04:50
0
Chimwemwe Zulu :
@yvonne
2026-10-20 10:23:51
0
To see more videos from user @achi.groundnuts, please go to the Tikwm
homepage.