@besterkanyenda22: #creatorsearchinsights #worshipinginchurch #viral #fyp #trending

BESTER
BESTER
Open In TikTok:
Region: MW
Tuesday 20 October 2026 10:40:08 GMT
39065
2544
503
124

Music

Download

Comments

user2015320037354
phalyc Austin :
Amen and amen [Pray][Pray][Pray][Pray][Pray][Pray]
2026-10-20 13:38:30
0
user34611939310237
Godfrey :
😭😭😭😭😭 why I'm not thankful for everything God did for me
2026-10-20 19:28:03
3
blessingswitness8
Blessings Witness :
ambuye awoneni ana anu ambuye
2026-10-20 18:38:20
0
mayesokachulu1346236
Blessings m Kachuku :
Mulungu awayendere anthu awa ,enafe maso akuluakulu ngt kadzidzi koma osayamika Mulungu
2026-10-20 22:57:00
0
nessah879
Nessah :
ambuye achitileni chifundo athu awa
2026-10-20 15:49:40
35
user96901665556550
Esimyshaibu :
Mulungu samalakwisad esh kukajambulitsa nyimbo km osaionela mulungu awasungila zabwino ku mwamba
2026-10-20 19:56:24
2
nancygm17
nancy gm17 :
mulungu ivani kulira kwa ana anu
2026-10-20 16:38:56
14
marykasiya4
marykasiya4 :
khopeyanu iwalire anthu awa ambuye
2026-10-20 16:16:06
1
bornlast55
Bornlast :
why am crying 😭 ambue achitilen chifundo ana anu🙏🙏🙏🙏
2026-10-20 15:57:01
12
twayamalichi1
ライリーTwaya Malichi :
Ngati ndamvela ndikuonela nyimbo yauthenga wabwino, ndiomvekaso ndi iyiyi. Wajambula nyimboyi, ndiyemweso wawathandiza anawa, ,, ndianthu omudziwa kum
2026-10-20 13:58:11
10
grolia560
grolia560 :
Amen and Amen ambuye apitilize kukudalitsani ana inu❤️❤️❤️🙏🙏🙏
2026-10-20 10:49:28
6
www.tiktok.com20122021
Glory Msuku :
Mulungu akudalitsen anyamata ndi atsikana
2026-10-20 16:50:27
2
chisomo.wa.mothiwa
chisomo wa mothiwa :
Chilanga school for the blind, ana amayimba bwino awa. Glory to the God
2026-10-20 18:50:09
2
patiencendawonash
patiencendawonash :
Ndili naye wanga Ali form 3 pano ku bt secondary xool osadandaura mlungu ndiwazatheka bwanji
2026-10-20 16:18:48
3
nyson.matebule
Nyson Matebule :
Mulungu wathu asamalileni anthu awa
2026-10-20 16:48:51
2
emilyphiri463
Emily Phiri :
why am i crying
2026-10-20 15:38:30
4
charlesth51
eruby 54th :
tiziyamikira chilingwedwe chathu aliyese adamurenga ndicholinga🙏🙏🙏
2026-10-20 13:54:53
2
mrsphiri2016
MRS D PHIRI :
Amen nkhope yanu iwalire ana anu anthu aone ukulu wanu
2026-10-20 16:01:08
1
eunice41702
Eunice :
amen
2026-10-20 11:30:56
1
matti_cherry
Matti Cherry :
what's the title of this song 🥹
2026-10-20 18:43:29
1
charitycharity140
charity charity :
amen mulungu salakwisa
2026-10-20 15:01:31
1
chisotigloria
chisotigloria :
😭😭😭akumbukiren Ana Anu Yahweh alandirenso kuona Monga munachita ndi Batomeyo
2026-10-20 17:43:04
1
berthawyson2
Bertha wyson :
Mulungu salakwitsad amen 🙏
2026-10-20 14:27:13
1
chrissymakhona
chrissymakhona :
ambuye ndiwabwino azibale anga
2026-10-20 13:43:29
1
twenty.kingz
Mena the Crop ScientistizZo🔥 :
yet I use my eye for blaa blaa. please 😭 God forgive me 🙏
2026-10-20 22:18:37
0
To see more videos from user @besterkanyenda22, please go to the Tikwm homepage.

Other Videos


About