uyu sikulina azakumana ndi munthu wa mtima osakanikila ndi manyi azamutizimula
2026-10-21 04:30:07
9
STEIN✍️ :
ichi ndi chi savage ichi
2026-10-20 19:19:46
26
user5581128437394cmatekenya :
nde mfumu yanji
2026-10-20 20:02:45
1
witika :
koma sopano iiiiiiiiiii maudindowa tafika nawo pena
2026-10-20 17:30:05
20
Ramos Jr✝️ :
This is not needed and why beating them…. U have authority already and with words they will listen… one day expect one of these people to sue you Bwana mayor.
2026-10-21 04:03:12
10
mimi vasco :
uyutu azakumana ndiwina azamukonza ndithu
2026-10-20 20:41:48
6
vizimiyeeee :
chimtengo pa motor yaine ine nde mukhoza kundimangatu 🤣
2026-10-20 18:54:27
10
bwiy :
azakumane ndineyo azandimanga koma apapa sipangathe bwino the way iknow the inner me
2026-10-20 19:59:44
1
chrispinerust :
pamene wafika malawipa akufunika iziz
2026-10-20 19:00:59
5
Dr Adaeze :
ìne angalandiretu judoo
2026-10-21 03:36:32
1
juliempingz❤️ :
nkona muli ndi mayor ogona
2026-10-21 09:59:10
0
O.B.k :
imagine it's Ur dad driving and you are in there then uziona akukwapulidwa 🥹
2026-10-21 04:11:27
4
Makeup by stephie💄👄 :
Koma kungacheme ine nde mnatopa kalekale 🤣🤣🤣🤣🤣🤣
2026-10-20 21:15:23
2
Mikhateees :
Zadala U Mayor mungamapatse mbuli, ndizimenezo Kaya osaphuzira zake ndindewu Malo osafunika ndewu
2026-10-20 21:57:38
4
eliza :
kulakwatu uku
2026-10-20 19:14:51
0
papanyox :
adzayesele ku Lilongwe aaaaaaa Ntchito imeneyo yofunika azipanga a police not iyeyo aaaaa
2026-10-20 19:45:22
0
To see more videos from user @badmakker, please go to the Tikwm
homepage.