comment section yadzadza ndi sister wake wa munthuyotu. What's going on
2026-10-22 07:58:03
0
Nafe C🌺 :
koma ngati akunena ndekutidi ndizoona...the good thing sis mwana wakura pitilizani kusamala and do business na mwana okanidwa amakhala ndi dalitso wa ndalama pa moyo wako push hard mama
2026-10-22 10:37:44
0
jimmy nkhoma :
iwe usadandaule ndikuthandiza pemphelo ndi loopya azakupepesatu ameneyo undipase number yako iyo ndi nchito yanga komanso ukoko tisokoneza ndi pemphelo 🙏🙏🙏🙏🙏
2026-10-22 08:27:03
0
Leah🥰 :
ngat inepano kundisiya ndmzimba ya 3 months pano alind 3yrs or 50kwacha ay pano ndnalimba mtima
chemwa musalimbane ndi anthu oti ali mbuyo mwanu mwanva? muchedwa nawo.ngat munasiyana that's all, backward never forward ever.Ex wanuyo ndi mkaziyo osewo akuoneka kuti ndiosowa zochita.
2026-10-22 05:01:38
0
Lindani Daud :
kungomuona beb chilipo chumusama ameneo
2026-10-21 12:18:06
0
L :
Maumboni ako ndiokayikitsa mama
2026-10-22 10:28:31
0
user9781561286236 :
ma post ako ukumayika nyimbo za milandu, take the point from there.
2026-10-22 11:32:03
0
SETEVE LANJESI 🇲🇼 :
mvuto ndilonti mumafuna kukwantiwa kwanukoko
2026-10-22 10:53:02
0
BALAKA :
😂😂😂😂..Gulugufe ameneyo ouluka Masana, Akukuchitila nsanje amawona Ngati uzivutika,uzimupembeza...wawona Kuti iweee Uli Cheteee... life goes on..no stress, just Brock the number basi
2026-10-22 11:34:43
0
Tony65 :
🙏🙏🙏
2026-10-22 03:19:11
0
thandiwe useni :
[Heartwarming][Heartwarming][Heartwarming]
2026-10-22 11:11:14
0
To see more videos from user @vingero1, please go to the Tikwm
homepage.