ine ndikufuna ma message a wap yakazanga adzilowa Ku wap wangaso
2026-10-26 10:42:38
0
Chifundo Alimon phakira :
imeneyo njiya ya yyitali ilipo ya simple
u don't need to have un app
2026-10-23 09:45:16
2
MABAD :
njila ya easy ndi netgurd bro application
2026-10-23 20:09:53
2
Chimuyz Lemani :
4ni yanga ndikakhara kt ndiseweresa zina zake munthu kundiimbira ku WhatsApp sikumawonesa paka ndipiteso kuwapuko vuto ndichani
2026-10-23 16:43:18
1
spellinah🥳🥳 :
ine phone yanga mulibemo freezer
2026-10-23 14:03:21
1
Haffiza Mtendere :
ine ndimphuxiseni munthu akatumiza msg ndikupanga delete isamantheke
2026-10-23 06:42:38
0
fatima jere :
kod ndingakapeze kuti app ameneka
2026-10-24 06:16:40
0
fahad :
ntchito yabwino ndithu
2026-10-24 10:56:16
1
georgebanda302 :
abwana ndikamatenga mavidiyo kuvitimeti kapena ku fasiti seva pamabwera zithu zoti ndizipanga inisito ndingapanga bwanj
2026-10-23 06:51:01
0
DyNamick 🤍🖤 :
Ngti app ya freezer mulibe
turn on proxy
and muike code iyii
1.1.1.1
mukhala mwapanga turn ghost mode
mukafuna kubwerera pa line turn off proxy🤝🏾
thankme later
2026-10-23 12:29:00
0
Husina Dawood ❤️❤️ :
2026-10-23 15:02:12
1
Dumisai Zidana :
🥰🥰🥰
2026-10-23 07:19:23
1
Faith Phiri :
🙏🙏🙏
2026-10-24 11:57:58
1
To see more videos from user @ityrksh, please go to the Tikwm
homepage.