@zakwathutv: Breaking: Zomvetsa Chisoni Kwambili Zachitika Pompano 8:30 AM Pomwe Tanker Yomwe Imatsitsa Mafuta ku Lilongwe Area 3 Pa Total Energies Yagwira Moto Ndipo Yaphulika Kupha Anthu Ndikuyatsa Magalimoto Omwe Anali Pa Line. (Video Yonse Link Ili Pa Profile) #FYP #malawitiktok🇲🇼
Zakwathu TV
Region: MW
Friday 23 October 2026 06:30:02 GMT
Music
Download
Comments
Lastborn :
mukuwona ngati tonse nda Tumbuka
2026-10-23 09:25:38
236
Brian FP Muleke :
ndy mkuzachita kulemba ku ai generated media aaah
2026-10-23 21:06:09
0
vinjel😍 :
😂Muonetsetse penapake anthu awili asanduka mmodzi ndani waona AI iyi
2026-10-23 08:28:40
547
Walu Kawonga :
this thing shall not happen in malawi in Jesus name
2026-10-23 07:46:57
436
Vashari Siwawa :
Ai how can two people become one person lie not true
2026-10-23 09:30:11
167
Andy Andrew :
How comes two people fall down and become only one person
2026-10-23 16:11:04
16
Layla Benedict :
folling two people stood one I wonder
2026-10-23 21:30:50
1
solnes transport..🇿🇼 :
MHSRP to those who lost there lives ...
2026-10-23 16:02:32
0
Teddy chimala :
A Malawi anayamba akuwako kuti fire kuno?
2026-10-23 15:19:06
9
Jane🇧🇼🇲🇼 :
ku lolingwe ndiye kuti☺️
2026-10-23 07:09:20
32
whee zombie :
koma Ai mukufuna makolo azitivuta ndimafunso
2026-10-23 07:56:03
14
7QBTS :
AI iyiyitu. Izizi nzofunika kumauza anthu aku Thekerani.
2026-10-23 09:59:49
8
Chriss painter :
Kod ndye kut Ai mwafika nayo pot muziwaona kuputsa anthu et
2026-10-23 08:57:53
9
Shreya Kamwetsa :
ndimaona ngt KU Lilongwe kwathu koma uku Ndiku Lolingwe
2026-10-23 11:01:54
5
otfchissper :
mayo khuno
2026-10-23 20:49:15
0
Enerst c paotan 💪💪 :
someone will going mad with your AI
2026-10-23 08:43:49
1
UNCLE M'MANGA :
Anthu oyipa olifunira dziko zoyipa basi eish
AI yimeyi zosakuthandizani.
Tiyeni tiziripempherera dziko lathu pazipsinjo zomwe tikudutsamozi🙏
2026-10-23 08:44:48
5
Keisha..🤎🤍💞 :
iiiesh
2026-10-23 07:22:16
1
Macpherson Tsilizani :
Zosakhala bwino ayi.
2026-10-23 06:54:45
7
Ama biiga :
AI
2026-10-23 17:20:56
1
rajiviiry :
jamani watanzania mpo mbona siwaono iku
2026-10-23 16:14:15
3
alex stevin :
nimeona wameanguka wawili ila alioamka ni Mmoja
2026-10-23 18:44:18
1
Miss Chilo💧 :
komano anthu awiri asanduka bwanji mmodzi
2026-10-23 19:17:02
3
Edward mkolesia :
Ai
2026-10-23 09:15:57
1
zahira's closet :
AI
2026-10-23 09:14:05
2
To see more videos from user @zakwathutv, please go to the Tikwm
homepage.
© 2021-2026 TikWM. All rights reserved.