nthaw Zina timafuna tisayakhe km don't joke nd bib
2026-11-09 19:07:49
0
Queen AISHA :
Chakwela mesa
2026-11-10 11:41:14
0
Victor Rashid :
adali wa petrol 😂😂😂😂😂❤️
2026-11-11 15:03:11
0
Gigi :
ndipo tambala ameneuja atangomaliza kulila a kongelesi anamuba😂
2026-11-01 17:51:17
7
Samson Banda :
wa chakwela
2026-10-26 08:10:13
6
Twaibu Amidu :
🤣🤣🤣🤣🤣 ine ndikuziwa anali wa chakwela mcp
2026-10-28 19:42:16
6
Joseph msuza :
Lazalo wa MCP ku Malawi
2026-10-31 21:00:03
1
𝗠𝗜~𝗞𝗔 :
Anali wa MCP tambala amene uja.
2026-11-01 22:22:15
1
Doyin😍 :
Anali wa Lazarus mu chichewa Lazalo
2026-10-26 20:42:48
4
SYLVESTER KABWIRI :
Ndi wa Chakwera tu
2026-10-27 19:56:45
1
aggiehax :
Kkkkkkkk ine ndimafuna dzina la mwiniwake bulu anamasula uja 🤣🤣🤣
2026-10-26 04:05:44
2
user8785115556104 desire :
chakwela ndiamen akudzwa
2026-11-05 06:59:28
0
Mudaziwani Chitemango :
🤣🤣🤣🤣 Anali wa mfumu Herod coz ndiomwe petro anakamukanila Yesu kkkkk bwanji ndakhozaa
2026-10-26 07:52:27
6
EMMANUEL DK MBEWE :
wa MCP
2026-10-29 20:25:20
1
musalah cedreck :
munuwake watamba uja ndi chakwela kkkk
2026-11-01 19:06:01
1
Moresi Feston :
active
2026-11-03 20:16:35
1
STAR~SHIP~TROOPER :
Za Mulungu osamabweretsapo nthabwala brother
Chifukwa cholinga cha Baibulo sichinali tambala, koma kukwaniritsidwa kwa uneneri wa Yesu. Yesu adanena kwa Petro mu Marko 14:30 kuti:
"Ndithu ndinena kwa iwe, kuti lero usiku uno, tambala asanalire kawiri, udzandikana ine katatu."
izi zinalankhulidwa pofuna kukwanilitsa zomwe Yesu Kristu anali akufotokoza kwa ophunzila ake ena osakhulupirila
2026-10-29 21:04:23
4
Hassan Allie :
still searching
2026-10-28 18:01:22
0
Alex Goeffery :
anali wa falawo
2026-10-26 11:50:39
3
user84692017939950 :
mu bible mulibe zimenezo nde ife tizitenga kt zoti tiyankhe
2026-10-26 19:20:12
3
cool man👞 # 0672098306 :
chakwel ndi kadz wake
2026-10-26 12:42:39
2
To see more videos from user @christhomy, please go to the Tikwm
homepage.